audio
stringlengths
43
45
text
stringlengths
0
24.1k
start_time
int64
0
1.83k
end_time
float64
1.74
1.85k
./data/chichewa-dataset\audio\segment_1.wav
Mawa atsikana tonse amene tangoyera mosadziwika bwinoamfumu ati tikakumane 12 koloko. Mawa, mawa, mawa, mawa, mawa atsikana inuyo makamaka inuyo, inu akuti atsikana tonse tangoyera mosadziwika bwino mbuyomo tidali okuda pano tangoyera mosadziwika bwino mawa tikakumane kwa Amfumu. Mawa, mawa, mawa atsikana tonse amene tidali okuda tangoyera 2 minitsi 3 minitsi omfumu akutifuna 12 koloko.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_2.wav
30
30.000188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_3.wav
zulo amama anaimba phone kufusa kuti mwana wanga alikuti ine pompo pompo kuthamanga kukatenga phone kuyamkhula nawo kuwafusa kuti mubwela liti kundiuza kuti abwela kumapeto kwa chaka chino nde ndauza owowo nde bwanji simunatitumizile zovala akuti atibwelesela akamabwela
0
26.029625
./data/chichewa-dataset\audio\segment_4.wav
Ndawonapo athu onyang'wa kwambiri zedi. amatama kwabasi. atatha kusosoka ngati silipasi. Dziko limatembenuka. Ndawonapo akazi okongola, kukongola kukutha. Nkhope zikuchita makwinya ngati mizere ya mbatata ndikumakhala. ndawonapo okondedwa athu achuma, chuma chikutha akuvala silipasi ina yayang'ana mbali ya uku ina mbali ya uku kumakhala koma mau a Yehova adzakhala mpaka muyaya. Ameni
0
26.965375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_5.wav
amwene ma project oti they can be done by malawians nde a ma project oti amalawi amatha kupanga ma project amenewo ndekuti ndalama zimakhalabe m'malawi momuno tilembanaso ntchito anthu koma upeza akupatsa ma china akubwelaso ma china ah aise ada e dziko lamunthu lino amwene
0
23.04
./data/chichewa-dataset\audio\segment_6.wav
Aliyese anamaliza sukulu basi. kaya analekeza sitandade 6 pamene anasiila iyepo ndipamene anamalizila iye.Anamaliza basi. osati kumanenana kumanena kuti enanu mukulephera kulemba chifukwa ee mwina mukulephera chifukwa simunapite ku sukulu aayii! aliyese anamaliza basi. Kaya wina anakafika ku university, anakamalizira mkoko. winanso analekezera sitandade 7 anamaliza chifukwa zifukwa zimene zinapangitsa iye kuti alekezere sitandade 7 ndi zimene zinamaliziranso iye sukulu. koma osamati iyayi mukulephera kulemba chifukwa simunamalize sukulu. Aliyense anamalizapa pa gulupupa. kaya analekera sitandade 3 anamaliza basi ameneyoyo. Zifukwa zimene zinapangitsa iye kuti alekele sitandade 3 ndi zimene zinapangitsa iyee kuti amalize sukulu yache. basi, so osamapangapo complain apa kumanena kuti eee mukulephera kulemba mwakutimwakuti mukupanga ma vn chakutichakuti. Ayi. ngati ukudziwa kuti ulibe unjeni data yokwanira iweyo sufuna kumvera ma vn siyaa! usatsegule vn uyisiye athu ena aitsegula ayivera. basi
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_7.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_8.wav
60
61.013375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_9.wav
ati a ati amakaikila ama amona ngati kuti mwina tungo mdoja kuti mwina mpandowo ungojambulidwa sukupangidwa and then nde eh atauona kunali ku ukhalilatu akangotele eh naisi chair akangotele nice chair ndamuuza kuti aha tapanga mani ndumenewotu mukanika nokha chifukwa choti mtengo sitikuvana hehe
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_10.wav
30
33.792
./data/chichewa-dataset\audio\segment_11.wav
Nseu wake uti uti?Nseu wake uti uti?Nseu wake uti uti?Nseu wake uti uti?
0
1.7415
./data/chichewa-dataset\audio\segment_12.wav
Ndie ndi mpatse zingati?Ndie ndi mpatse zingati?
0
2.71675
./data/chichewa-dataset\audio\segment_13.wav
Ulendo wa ku maliro watalika kwambiri, akanangotegalatu katundu wawo kuti angopitilatu.Ulendo wa ku maliro watalika kwambiri, akanangotegalatu katundu wawo kuti angopitilatu.
0
6.130125
./data/chichewa-dataset\audio\segment_14.wav
Kodi a Keli umbetawu mpaka liti, musakhaletu omakwatiwa usiku. Ngati zikuvuta tauza abusa akupempherereniKodi a Keli umbetawu mpaka liti, musakhaletu omakwatiwa usiku. Ngati zikuvuta tauza abusa akupempherereni
0
7.523313
./data/chichewa-dataset\audio\segment_15.wav
Mesa inunso munakwatiwapoMesa inunso munakwatiwapo
0
2.461375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_16.wav
Zoona ndithu. NdizothekaZoona ndithu. Ndizotheka
0
2.298813
./data/chichewa-dataset\audio\segment_17.wav
Azipita kwawo awa inuAzipita kwawo awa inu
0
2.507813
./data/chichewa-dataset\audio\segment_18.wav
Tsono ukuseka chaniTsono ukuseka chani
0
1.7415
./data/chichewa-dataset\audio\segment_19.wav
adye mazila 16 otsalawoadye mazila 16 otsalawo
0
2.92575
./data/chichewa-dataset\audio\segment_20.wav
Nde anthuwo akutanipo?Nde anthuwo akutanipo?
0
2.368438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_21.wav
Zachitikanso kachikena lero?Zachitikanso kachikena lero?
0
2.74
./data/chichewa-dataset\audio\segment_22.wav
basi akangokazingira tomato azikadya ngati ndiwo kwawo basi akangokazingira tomato azikadya ngati ndiwo kwawo
0
4.435063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_23.wav
Koma anthu enawo sakuonetsa chidwi nanga tikungokhala ngati awiri fe ndiamene tikutengapo gawoKoma anthu enawo sakuonetsa chidwi nanga tikungokhala ngati awiri fe ndiamene tikutengapo gawo
0
11.331375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_24.wav
kabudulayu wasokedwa kuti ameneyu?kabudulayu wasokedwa kuti ameneyu?
0
3.065063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_25.wav
Pepani, simunalinso ku Maliro pakatipa. Tipeleka ya chipepeso yo.Pepani, simunalinso ku Maliro pakatipa. Tipeleka ya chipepeso yo.
0
5.851438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_26.wav
Mawa ndikupita kumudzi ku maliro a Phiri, achimwene obadwa kwa agogo akuluMawa ndikupita kumudzi ku maliro a Phiri, achimwene obadwa kwa agogo akulu
0
5.596063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_27.wav
Mwaswera bwanji?Mwaswera bwanji?
0
1.811188
./data/chichewa-dataset\audio\segment_28.wav
Ndikawapatsa 10000 inayo ndiyendere Ndikawapatsa 10000 inayo ndiyendere
0
3.901
./data/chichewa-dataset\audio\segment_29.wav
Ngati zakudya zimavuta munthu wapa ntchito nde munene mwana wa sukulu Ngati zakudya zimavuta munthu wapa ntchito nde munene mwana wa sukulu
0
4.388625
./data/chichewa-dataset\audio\segment_30.wav
Ikapezeka ina munena, kapena anzanu ena otchipa, koma ikufunika yambiriIkapezeka ina munena, kapena anzanu ena otchipa, koma ikufunika yambiri
0
5.99075
./data/chichewa-dataset\audio\segment_31.wav
Ndipanga Monday ndinapita ku school kwa mwana nde ndabwera mochedwaNdipanga Monday ndinapita ku school kwa mwana nde ndabwera mochedwa
0
4.713688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_32.wav
Nde ikapezeka ndalama ina mundiuzaNde ikapezeka ndalama ina mundiuza
0
3.041875
./data/chichewa-dataset\audio\segment_33.wav
0
3.599125
./data/chichewa-dataset\audio\segment_34.wav
Akuuzani kuti muzimitse ma phone tsopano?Akuuzani kuti muzimitse ma phone tsopano?
0
2.832875
./data/chichewa-dataset\audio\segment_35.wav
Ukapeza munthu oti akufuna makwacha ndimafuna andilipirire galimotoUkapeza munthu oti akufuna makwacha ndimafuna andilipirire galimoto
0
5.270938
./data/chichewa-dataset\audio\segment_36.wav
Mugwiritsa ntchito ya kwa Nsapato kapena ya anangozo?Mugwiritsa ntchito ya kwa Nsapato kapena ya anangozo?
0
3.274063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_37.wav
Galimoto ya ndani?Galimoto ya ndani?
0
1.76475
./data/chichewa-dataset\audio\segment_38.wav
Akupanga ndalama zingati?Akupanga ndalama zingati?
0
2.229125
./data/chichewa-dataset\audio\segment_39.wav
Kuti ndiyambe kuzitchula pano muthanso kudabwa.Kuti ndiyambe kuzitchula pano muthanso kudabwa.
0
3.413375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_40.wav
Mutu wake sukoka kweni kweniMutu wake sukoka kweni kweni
0
2.600688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_41.wav
Nanga munthu kutsamzika ife tisanamalize kujama. Amatero?Nanga munthu kutsamzika ife tisanamalize kujama. Amatero?
0
4.66725
./data/chichewa-dataset\audio\segment_42.wav
Lero nde ndathamanga kwambiriLero nde ndathamanga kwambiri
0
3.065063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_43.wav
Mawa ndikufuna ndipite kumudzi ndikawaone mayi angaMawa ndikufuna ndipite kumudzi ndikawaone mayi anga
0
4.388625
./data/chichewa-dataset\audio\segment_44.wav
Panopa upite kaye ku sukulu ukaweruka ukadutsire ku msika ukagule ndiwoPanopa upite kaye ku sukulu ukaweruka ukadutsire ku msika ukagule ndiwo
0
8.31275
./data/chichewa-dataset\audio\segment_45.wav
Kodi Khama yo akutani?Kodi Khama yo akutani?
0
2.34525
./data/chichewa-dataset\audio\segment_46.wav
Ife zimenezo kwathu sitimadya chifukwa palibe amene amazikondaIfe zimenezo kwathu sitimadya chifukwa palibe amene amazikonda
0
5.851438
./data/chichewa-dataset\audio\segment_47.wav
Iwe idya kaye nsimayo ukamaliza ndikutuma ku chigayo ukagayitse chimangaIwe idya kaye nsimayo ukamaliza ndikutuma ku chigayo ukagayitse chimanga
0
7.175
./data/chichewa-dataset\audio\segment_48.wav
Kunyumba kwathu kwabwera alendo a amuna ndi a akazi ndi kamwana kakang'ono ati abwerera kwawo mawaKunyumba kwathu kwabwera alendo a amuna ndi a akazi ndi kamwana kakang'ono ati abwerera kwawo mawa
0
9.009375
./data/chichewa-dataset\audio\segment_49.wav
Ife tidzabwera chaka chamawaIfe tidzabwera chaka chamawa
0
2.92575
./data/chichewa-dataset\audio\segment_50.wav
Ndikupita kukaona ine ndatopa kwambiri leroNdikupita kukaona ine ndatopa kwambiri lero
0
3.483
./data/chichewa-dataset\audio\segment_51.wav
Ndi ndani wakumenya iweyo leroNdi ndani wakumenya iweyo lero
0
2.71675
./data/chichewa-dataset\audio\segment_52.wav
Tiyeni tibwerere kumene tachokeraTiyeni tibwerere kumene tachokera
0
2.693563
./data/chichewa-dataset\audio\segment_53.wav
Tayatsaniko ma kendulo kuli mdima kuchipinda kuno.Tayatsaniko ma kendulo kuli mdima kuchipinda kuno.
0
4.288
./data/chichewa-dataset\audio\segment_54.wav
Bweretsani ndiwozo mwana adye nsima adzigona.Bweretsani ndiwozo mwana adye nsima adzigona.
0
4.096
./data/chichewa-dataset\audio\segment_55.wav
Ana amuna alipo angati.Ana amuna alipo angati.
0
4.032
./data/chichewa-dataset\audio\segment_56.wav
Tapita ukandigulile mankhwalaTapita ukandigulile mankhwala
0
2.74
./data/chichewa-dataset\audio\segment_57.wav
Madzi akumwa mumakatunga kuti nthawi zambiri.Madzi akumwa mumakatunga kuti nthawi zambiri.
0
5.056
./data/chichewa-dataset\audio\segment_58.wav
Nyumba yanu ili ndi zipinda zingati.Nyumba yanu ili ndi zipinda zingati.
0
3.712
./data/chichewa-dataset\audio\segment_59.wav
Mawa kugwa mvula yochuluka.Mawa kugwa mvula yochuluka.
0
4.032
./data/chichewa-dataset\audio\segment_60.wav
Sindikumva bwino, ndadwalaSindikumva bwino, ndadwala
0
2.856063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_61.wav
Ngati sitipanga zimenezi chathu palibepoNgati sitipanga zimenezi chathu palibepo
0
4.109938
./data/chichewa-dataset\audio\segment_62.wav
Munthu akufuna chani?Munthu akufuna chani?
0
2.9025
./data/chichewa-dataset\audio\segment_63.wav
Kodi ena amakhulupililasoKodi ena amakhulupililaso
0
3.483
./data/chichewa-dataset\audio\segment_64.wav
Koma ma potholes ali Kwathu ku Naperi uku umachita kuda nkhawa ukamabwerera kunyumba tu. Koma basi timangoyendera mwambi omweuja "okumba fulu sakuda nkhawa"Koma ma potholes ali Kwathu ku Naperi uku umachita kuda nkhawa ukamabwerera kunyumba tu. Koma basi timangoyendera mwambi omweuja "okumba fulu sakuda nkhawa"
0
13.723
./data/chichewa-dataset\audio\segment_65.wav
Iwe tabwela kuno Iwe tabwela kuno
0
2.879313
./data/chichewa-dataset\audio\segment_66.wav
Awawa ndi azinzanga ndipo ndi mabwana koopsa. Koma pa uwiri wawo palibe angathe kusintha ma gear a motha olo ya automaticAwawa ndi azinzanga ndipo ndi mabwana koopsa. Koma pa uwiri wawo palibe angathe kusintha ma gear a motha olo ya automatic
0
8.448
./data/chichewa-dataset\audio\segment_67.wav
Ndawauza abwana anga ndudwalaNdawauza abwana anga ndudwala
0
3.584
./data/chichewa-dataset\audio\segment_68.wav
Nseu wake uti uti?Nseu wake uti uti?
0
2.432
./data/chichewa-dataset\audio\segment_69.wav
Tingopepesa bwanji kuti nkhaniyi isapite pataliTingopepesa bwanji kuti nkhaniyi isapite patali
0
4.096
./data/chichewa-dataset\audio\segment_70.wav
muzitikhululukira..musatope nafe kutitumizira zithuzomuzitikhululukira..musatope nafe kutitumizira zithuzo
0
6.72
./data/chichewa-dataset\audio\segment_71.wav
Kumayamika mulungu wakumwambaKumayamika mulungu wakumwamba
0
2.944
./data/chichewa-dataset\audio\segment_72.wav
Muli ndi zaka zingati?Muli ndi zaka zingati?
0
2.752
./data/chichewa-dataset\audio\segment_73.wav
Woyankha mafunso ndi mwanuna kapena mkazi?Woyankha mafunso ndi mwanuna kapena mkazi?
0
4.672
./data/chichewa-dataset\audio\segment_74.wav
Kodi munabadwa liti?Kodi munabadwa liti?
0
2.432
./data/chichewa-dataset\audio\segment_75.wav
Ndikumenyatu iwe Ndikumenyatu iwe
0
2.113063
./data/chichewa-dataset\audio\segment_76.wav
Ndinjira yanji yeniyeni imene mumapezera ndalama?Ndinjira yanji yeniyeni imene mumapezera ndalama?
0
4.224
./data/chichewa-dataset\audio\segment_77.wav
Kodi nyumba imene mukukhalayi ndi yanu kapena ndi ya lendi?Kodi nyumba imene mukukhalayi ndi yanu kapena ndi ya lendi?
0
4.864
./data/chichewa-dataset\audio\segment_78.wav
Ufulu wokhala ndi moyoUfulu wokhala ndi moyo
0
2.176
./data/chichewa-dataset\audio\segment_79.wav
Anthu SAYENERA kusala anzawo potengera chigawo, mtundu, kukhala mwamuna/mkazi, chipembedzoAnthu SAYENERA kusala anzawo potengera chigawo, mtundu, kukhala mwamuna/mkazi, chipembedzo
0
8.768
./data/chichewa-dataset\audio\segment_80.wav
Anati chani a landlord mutapeleka rent tsiku lisanafike?Anati chani a landlord mutapeleka rent tsiku lisanafike?
0
4.544
./data/chichewa-dataset\audio\segment_81.wav
Mutha kumadyatu ma peyalawa, zipatso zimathandiza mthupi Mutha kumadyatu ma peyalawa, zipatso zimathandiza mthupi
0
5.12
./data/chichewa-dataset\audio\segment_82.wav
0
2.496
./data/chichewa-dataset\audio\segment_83.wav
Kuyambila lero anthuwo muziwapanga Kaye remove mpaka mutawapepesaKuyambila lero anthuwo muziwapanga Kaye remove mpaka mutawapepesa
0
5.76
./data/chichewa-dataset\audio\segment_84.wav
Eyetu nanga azimvaEyetu nanga azimva
0
3.008
./data/chichewa-dataset\audio\segment_85.wav
Kodi Adam anali kuti?Kodi Adam anali kuti?
0
2.048
./data/chichewa-dataset\audio\segment_86.wav
Koma lero nde mvula yagwa yambiri Koma lero nde mvula yagwa yambiri
0
3.227625
./data/chichewa-dataset\audio\segment_87.wav
Tazimitsako magetsiwo Tazimitsako magetsiwo
0
2.56
./data/chichewa-dataset\audio\segment_88.wav
Pa lunch udya chani lero?Pa lunch udya chani lero?
0
5.184
./data/chichewa-dataset\audio\segment_89.wav
Mayi ako apita kuti?Mayi ako apita kuti?
0
5.76
./data/chichewa-dataset\audio\segment_90.wav
Bambo ako apita kuti?Bambo ako apita kuti?
0
3.84
./data/chichewa-dataset\audio\segment_91.wav
Nthawi ili bwanji pano?Nthawi ili bwanji pano?
0
4.416
./data/chichewa-dataset\audio\segment_92.wav
Upite kunsika ukagule ndiwoUpite kunsika ukagule ndiwo
0
4.736
./data/chichewa-dataset\audio\segment_93.wav
Umuyimbileko phone Kondwani, umuuze abweleUmuyimbileko phone Kondwani, umuuze abwele
0
7.936
./data/chichewa-dataset\audio\segment_94.wav
Akabwela a bambo ako uwauze ndapita kunsika kukagula ndiwo.Akabwela a bambo ako uwauze ndapita kunsika kukagula ndiwo.
0
7.296
./data/chichewa-dataset\audio\segment_95.wav
Undigaileko k5000 kwacha Undigaileko k5000 kwacha
0
5.184
./data/chichewa-dataset\audio\segment_96.wav
Nde mwati zinakhala bwanji Nde mwati zinakhala bwanji
0
3.776
./data/chichewa-dataset\audio\segment_97.wav
Mudzapha munthu za ziiiMudzapha munthu za ziii
0
3.575875
./data/chichewa-dataset\audio\segment_98.wav
Chavuta ndi chani kodi?Chavuta ndi chani kodi?
0
3.84
./data/chichewa-dataset\audio\segment_99.wav
Mumpatse moni Anafe yo Mumpatse moni Anafe yo
0
5.632
./data/chichewa-dataset\audio\segment_100.wav
Ukutani Kodi? Tasiya zimenezo Ukutani Kodi? Tasiya zimenezo
0
4.928
README.md exists but content is empty.
Downloads last month
40