audio
stringlengths 43
45
| text
stringlengths 0
24.1k
| start_time
int64 0
1.83k
| end_time
float64 1.74
1.85k
|
---|---|---|---|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_201.wav | 1,260 | 1,290 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_202.wav | 1,290 | 1,320 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_203.wav | 1,320 | 1,350 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_204.wav | 1,350 | 1,380 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_205.wav | 1,380 | 1,410 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_206.wav | 1,410 | 1,440 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_207.wav | 1,440 | 1,470 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_208.wav | 1,470 | 1,500 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_209.wav | 1,500 | 1,530 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_210.wav | 1,530 | 1,560 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_211.wav | 1,560 | 1,590 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_212.wav | 1,590 | 1,620 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_213.wav | 1,620 | 1,650 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_214.wav | 1,650 | 1,680 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_215.wav | 1,680 | 1,710 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_216.wav | 1,710 | 1,740 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_217.wav | 1,740 | 1,770 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_218.wav | 1,770 | 1,800 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_219.wav | 1,800 | 1,823.299063 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_220.wav | Aah tili kuno kwa a Nsangwa komaso a gulupu a Nsangwa, T/A Kayembe ndipo tikucheza ndi abambo amene akhala akugwiranawo nchito za CARE kuno ku Dowa. Nfunso loyamba a zibambo mwakhala mukutengapo mbali kodi mwakhala mukutengapo mbali pa project ya CARE kuno kwa Kayembe? Mwakhala mukutengapo gawo? Eya takhala tikutengapo nawo mbali, chabwino. Ndi ntchito ziti zimene mwakhala mukutenga nawo mbali zokhudzana ndi CARE? Ntchito zilipo zingapo ine ndingotchulapo ziwiri, ngati madyedwe abwino kuwana achichepere oyambira miyezi kulekeza zaka five komaso kuphunzitsana za gender. Za gender? Eya., chabwino. Zilipo zina tikupanga kunoko zimene a number one wa sadatchule? Zowonadi zilipo zina zomwe tikupanga kukhudzana ndi za ukhondo pakhomo, nde kuti mwana asana asanalandire chakudya kunsambitsa kunsambitsa komaso iwe wamkulu kusamba manja mkumpangira chakudyacho kuti mwanayo adye, Komaso zina zowonjera pamenepo zina zomwe anena kale azangawa zina mwa izo ndi zimenezi. Chabwino awo ndi mau a number five paliso zina zomwe mwina sizinatchulidwe zomwe tikupanga nawo? Nde tikamayankhula tidzitchula nambala yathu kuti tigwire nambalayo. Ah ine ndine namabala folo nufuna nifotokozere zokhudzana ndi gender, gender imatanthauza kugwira ntchito moganizirana pakati pa mamuna ndi mkazi. Ineyo natengapo mabli mu Polojekiti pokhudzana pogwiritsa ntchito udindo umenewu Zikomo. Ine ndine nambala two ehe gender imatiphunzitsa kuti tidzikhala tose pamodzi pokhala udindo okhiudzana amayi ndi abambo mofanana, chabwino, Zikomo.
Enafe tuti chani? Apapa za gender za fotokozeredwa mkutheka tufuna tifotokoze za ma gawo ena aja. Ineyo ndine namabala six ndufuna ndifotokozere mene bungwe la CARE latitandizira kumbali ya za ukhondo,zaukhondo monga dzimbuzi, mbuyo mu anthu ambiri amakanyera ku thchire Panopa chifukwa chakubwera cha CARE atithandiza kuti aliyese akhala ndi zibudzi makomomu ndipo ukhondo usamalika kwambiri makomo mwathumu zikusamalika kwambiri matenda so monga cholera aluchepa chifukwa tili ndi zimbudzi. Matchire adatha itha anthu aiwuvetsatsa kukhala ndi zimbudzi makomo mwathu Zikomo. Ine ndine nambala fili ndi,mafunaso ndi yankhulepo zokhudzana ndi pulojekiti ya CARE, mbuyomu CARE isanabwere tinali ndi mavuto akunyentchera kwa ana koma kubwera kwa CARE idatilimbikitsa kuti tiphunzire madyebwe abwino monga ngati kumbali ya ya wana. Panthawi yomwe CARE yakhala ikutiphunzitsa kufika pano atapindula ngati kuno kwa Nsangwa ana akukulaso bwin Zikomo kwambiri.. Mwaphunziro zotani anambala fili mu nkhani ya madyedwe abwino kuchokera ku CARE? Munkhani ya madyedwe abwino munthawi yomwe CARE isanabwere timangoti ana mwina kukacha osawapatsa kachakudya kena kalikose komwe katha kuwapatsa mphanvu muthupi mwao koma CARE itabwera imatiphunzitsa zinthu zimene ifeyo sitimatha kuchidziwa kuti ah kodi kachipatso aka titapatsa mwana katithandiza chakuti komano kufika pomwe tinayamba kuphunzira ndi a CARE tatengapo mbali yochuluka moti ana ayi ndithu tikamawatumiza ku school ya mkaka alumapita mosangalala chifukwa cha CARE. Chabwino tipite patsogolo pangÕono inu ndi azibambo tsopano azikazi anu amapanga zotani ndi a CARE? Kapena zimene mwafotokoza apazi mapangira limodzi ndi azikazi anu? Ine ndine nambala one ngati mabanja athu muthawi imene bungwe la CARE labwera mu 2017 kuyamba kudzatiphunzitsa , kwakukulu maphunzitsos athu timalandirira pamodzi ngati mudzi mkomaso ngamabanja., zakadyedwe kabwino komaso za ukhondo komaso kulimbitsa ana achichepere kuti adzipita ku school komaso kulimbikitsa ana asungwana kuti asakwatiwe ali ndi zaka zochepa kuti afikire pa msikhu wao, chabwino pamenepo zaveka zikuoneka kuti zose mwaphunzira pamodzi eti? Mmmm . Ngati pamakhala ntchito, nthitozi magwira limodzi ndi a CARE inu ndi azimayi eti? Ehe chabwino. Tiyeni tipite patsogolo, kusintha kumene kwachitika mkotani kumbali ya madyedwe komaso kumbali ya ma udindo abambo ndi amayi amene tikuti gender eti? Eya timafuna mufotokoze kuti kusintha kwake ndikotani? Munayamba kale kufotokoza. Ine ndi namabala fili kuno kwathu kusadabwere CARE tingoyerekeza kuti VHC timatheka kuti mipando ngati imene ija timayikakamiza kwa azibambo okha okha, mwina azimayi kuyikamo awiri koma itabwera CARE tidakapezeka kuti otsogolera mwina mipando imeneyi kukapezeka kuti mzimayi alipatsogolo pa anthu amuna. Olo VDC yakuno kwathu ndiye kuti pano tukamba pano chairman wa VDC yo ndekuti ndi mzimayi chifukwa cha umphungu umene CARE idatani? Idabweretsa idatiphunzitsa zinthu zomwe sitimazitani? sitimazidziwa. HHC mamatanthauzira bwanji ? Village Health Committee.Chabwino, ena tingafotokoze bwanji zaku sintha komune tonani chibwerereni a CARE kuno ? Kusintha, ine , ndine namabala two kusintha kwa Care yabwera kuno kwasintha zinthu zango zingapo zokhudzana ndi zomwe tikuti madyedwe abwinowa komaso kuti ana kuwalimbikitsa kuti aziapita ku school komaso asamakwatiwe zaka zili zochepa aziyamba ayamba kupita ku school ndipo atachoka kumeneko akatsiriza school ndiye adzizipeza mabanja, sitilora adzikwatiwa ali ndi zaka zosakwana eyitini . zimenezi maphunziro kwa aphunzitsi a CARE? Eya, enanu muti bwanji? Taona kusintha kotani? Mwina mkutheka wina atha kunena kuti ine sinaoneko kusintha, mwina ahaa zinthu zaipa sizikukhalaso bwino tiyeni timasuke ndithu tinene ndithu. Ine ndine number five mfuna neneko zomwe CARE yasintha kuno kwa Nsangwa, group Nsangwa, masiku ambuyowa CARE isadabwere makomo makhala matchire ochulukitsako komaso ana amaonongeramo koma kufika kwa CARE idadzatiphunzitsa zaukhondo kuti pakhale madyedwe abwino ndaona kuti mudzi wathu uno wa Nsangwa wasintha ndithu moti mwachimenechi chimene CARE ndaona yatisinthirako kuno kwa Nsangwa Zikomo. Paliso zina zowonjezera pamenepo zofotokozera zosintha kwa miyoyo yathu pakubwera a CARE? Chabwino, zilipo zimene titha kunena kuti sizidasinthe titha kufotokozera?
Ine ndi nambala one zedi mpakuti mwina sizingatheke kuti mzaka zochepa kapena ziwiri zitatu kuti zili zose kusinthiratu kapena kutheratu ayi, koma ngati mudzi munomo mwa Nsangwa zambiri zasintha madzi abwino tili nawo komaso ukhondo uli pakati pathu komaso ana kunyentchera ahh sionyentchera kweni kweni tingoti kudatheratu kunyetchera koma chimene tikhoza kunana kuti sichinasinthe ni mwina kuchuluka kwa chiwerengero cha wanthu ngati madera ogundizana ndi a gulupu answangwayi madzi ngati amene a CARE adalonjeza kuti adzakhala mkanthawi kena kokonza mijingo yowonongeka kapena kukumba mijigo nu jiwona kuti a CARE atipangira kusasintha kwake titha kuti mwina sizinasinthe zimenezo. Poyamba paja munanena kuti tikumwa madzi abwino , adakumba mijigo yake? A CARE sadakumbe mijingo kapena kukonza mijigo yowonongeka koma mudzi mwathu muno tili ndi jingo. Jigo? Eya . nde mene mati mukumwa madzi abwino madzi abwino amenewa anabwera bwanji? Anabwera ndi a CARE? Kapena bwanji? Ayi anabwera ndi a Concern Universal , chabwino, eya timafuna tinvetsetse pamenepo eya chabwino. Aah ine ndine number two kusintha kwina ndiku gawo la gender, gender yatisinthitsa kuti miyambo ina tiyisiye kukhudzana ndi kulowa kufa kukhudzanaso kuti izi tadya Kamba koti ndi oyembekezera adzakhala mwana opanda tsitsi zimene zija, miyambo imene ijakuti idatha kukhudzana ndi kaphunzitsidwe ka CARE komaso zokhudzana ndi kulowa kufa zosezo zidatha chifukwa miyambo yoseyo idali yolakwika imene imatsatidwa kale. Pano timalora kuti munthu azichita zinthu madyedwe abwino kuti pakhomo pakapezeka zchakudya tose tidzidya mofanana osasankha kuti ichi ncha bamboo ichi mchamayi Zikomo. A number one nanafotokozapo za kutha kwakunyentchera eti? Eya, Ndi ziti zimene mwatengapo Care zathandizira kuthetsa kunyetchera? Ahh gawo limene tatengapo? Ngati Kuphunzitsidwa kupeza zinthu zina zimene zikhoza kumuthandizira mwana kuti akule ndi thanzi pamene wabadwa kufikira pa nsinkhu oleka kuyamwa ngati kumuyamwitsa mwakathuthi mosalekeza komaso kumudyetsa phala mwana uja mawa, masana, madzulo komaso kupita naye ku sikelo pafupi pafupi, pamene ngatipilojekiti ya CARE isanabwere ndi pulojekiti ya SUN zimenezi anthu adalibe umphungu wabwino mwina mwana akabwadwa mwina amakabadwira kwa zamba amgakhale ku sikelo osapita. Kuphunzira kuti madyedwe abwino ndi awa kunalibe nchifukwa ana ake pomakula amakula okwinimbira chifukwa amatheka kuti wabadwira ku mzamba angakhale ku chizungu osapitako ayi. Tathokoza number one. Number three zinthu zimene tazipeza ngati kupindula ngati ndimene mwafotokozera ndi kapezedwe kazinthu zimene tikhoza kuthetsera kunyetchera, kalelo timava kuti zinthu zake ndi zochita kugula koma CARE idadzatiphunzitsa kuti zinthu zina ziliko zimene kuno kumudzi timakhala nazo koma chifukwa chosaphunzitsidwa zinthizi zimaoneka kuti ndizosatheka pakadyedwe kabwino nde itabwera CARE idadzatiphunzitsa zinthu monga kulima tidimba tamakomo munthawi ya dzuwa kuti tidzikhala ndi ndiwo ngat za masamba. Zinthu zimenezo kalero timaziona zinthu zozira koma itabwera CARE tidazitenga zinthu zofunikira ndipo ikafika nyengo ya dzuwa timalima timadimba ndipo ndithu tindiwo tosintha sintha timadyetsa ndithu ana kuti zinthu ziziyenda mofunikira. Madimba tulima madambomu kapena makomomu? Timadimba timeneto matiuza kuti tidzilima makomomu monga ngati nthawi ya dzuwayi, ndiye anakuphunzitsani? Eya chabwino tuthokoza. Kutheka mwinaso enaso ali ndi zowonjera tisanapite patsogolo?mm ine kuonjezera kwanga ine ndine number four kuonjezera kulipo konga ngati kufotokozera kukhudzana ndi madyedwe abwino, pali zinthu zina zimene timaziona ngatikuti sizinthu zoti zingatithandize titamadya koma pobwera kwa CARE nikutizindikiritsa pa zinthu zomwe titha kudzilimira ngati soya, ngati maungu nyemba kumene zowona ngati soya abungwe la CARE atiphunzitsa kuti tikhoza kumapanga mkaka kumamwa bwino bwino, dzungu kupanga sitoko bwino bwino, nkhwani kuphikira ni mazira ngati snack kumadya bwino bwino cholinga zimenezi titamadya matupi athu mudzikhala bwino kapena wana wathu akamadya zinthu zimenezi adzikhala ndi mphanvu Zikomo. Chabwino, ayi tathokoza tiyeni tipite patsogolo, ndimavuto otani omwe inu kapena ena akukumana nawobe pa zamadyedwe oyenera mako komaso mudzi mudzi muno? Aah ine ndine wanambala two mavuto amene alipo niulima mochepekera koma pakhomopo osamapeza chakudya chokwanira bwino ndiye kuti pakhomopo pamakhala povuta kuti chidzikhala pa limiti yake patsiku. Zikumakhala bwanji kuti apezeka alima mochepekedwera? Komwe kumakhala kovuta kwambiri nkapezedwe ka fetereza mindaso malingana ndi kuchulukana ndiyongodulirana timizere miere ninyengo mene ikuyendera pena pake ukakonzekera nyengo ija sili kuyenda bwino , mbeu zija zikukanika makulidwe abwinokukabwera dzuwa. Komaso kanthawi kena kumabwera mvula yochuluka ndiye kuti malo omwe ali odikha ndekuti mbeu zija zikumapita madzi. Ndimavuto ena ati anthu akukumana nawo amene akukumana nawo angakhale a CARE akugwira ntchito? Mavuto okhudzana ndi madyedwe abwino? Number five mavuto amene takumana nawo ngati ife anthu akuno kwa Nsangwa CARE ili mkatimu ndi anjala. Moti njala ndi chinthu chimodzi chomwe chimalepheretsaso kuti tikwaniritsetso kuti ana athu adzidya bwino, koma maphunziro a CARE titaphunzira kale, tudziwa zakudya zomwe anawo atha kumadya ngati kuno kumudzi Zikomo. Chabwino, ena tikuti bwanji? Anthu akukumana ndi mavuto otani kumbali ya madyedwe,ngakhale a ACARE amagwira ntchito kuno? Ine ndine number one, mavuto Yamane yalipo pamene bungwe la CARE lilimkatimwemu mavuto yomwe yalipo yomwe nuli waona kapena yomwe anthu amawaona mwina nikusanvetsetsana pakati pa mkazi ndi mamuna. Zomwe zija takamba kale kuti gender pali mabanja ena angakhale chakudya kuchipeza chokwanirana koma malamulo ndi yamene amakulapo pabanja paja kufika poti mwina anthu kuphika kumaphuika monyanyalitsana kapenakumaphika moperewera. koma mavuto amenewa analipo mkati mkatimu kwambiri kumbuyoku a CARE asanabwere koma Panopa tuona kuti zachepa ndithu mavuto yamene nimawaonako nawamenewa koma Panopa yachepa chifukwa chophunzitsidwa. Chabwino.
Paliso zina zowonjezera pamenepa? Ndine number five choonjerapo chilipo maka maka ku nkhani ngati ija munatchulako maka maka azanga anambala one ya madzi, madzi ndiye satikwanira chifukwa mudzi wa Nsangwa ndi waukulu kwambiri muli anthu ochuluka. Muli makomo angati mudzi mwa o Nsangwa? Mudzi mwa Nsangwa angakhale chiwerengero chamakomo sicikudziwika bwini bwino ayi koma mukuona kwangwa muli makomo yochuluka ndithu yoti akhoza kupitilira five hundred. Ndiye mijingo ilipo ingati? Jingo tilinawo umodzi okha basi. Chabwino. Nde mbali yomwe amagwiritsira ntchito jigowo mukhoza kuona kuti madzi abwino alinawo koma mbali ina ndiye kuti kulibeko madzi abwino, chabwino. Ndangochitapo chidwi pamenepo mwaqkamba za jigo amene amasamala ku jingo ndi ndani? Abambo, amayi kapena nose pamodzi? Ine ndi number six? Masamalidwe apa jingo zimayimira mayi ngakhaleso zibamboo. chabwino chifukwa kuti jingo uja sangapange chitukuko yekha mzimayi ayi, magwirizana kukatenga minyala mubweretse pamene paja nde kuli a comeettee, comet imakhal zomwe tikamba za gender kuti kukhla azimayi uku kukhla azibambo ndemasamalidwe apa dirawo apa jigo zikuyimira mbali zose , chabwino. Mkazi ngakhale mamuna.Chabwino. Number one munali ndi zowonjezera? Ine ndine number one nimangofuna ndionjezere zimene a number five akamba , mudzi uno wa Nsanga ulidi ndi mabanjadi ochulukirapo pafupi fupi fafandede chakuti, mudzi uno ndi umene mwauonawu kuchoka kumapeto uku kukafika kumapeto uko ndiyeno timangolumpha kumudzi kena kake apa tili ndi mudzi winaso apo oti umangotetezekako nthawi ino ya mwavu uno. Pa Nsangwa two mapene . umangotetezeka kunthawi ya dzinja ino yimene imapezako madzi yozipezera yapa chithaphwi koma kuyambira july mpakana kukafika December jigo umagwira ntchito ndi omwewo ndiye mumadziwa madziwo amafika poti amatha. Chabwino, ndi mavuto amene takumana nawo pamene CARE ikugwira ntchito ndi amenewo, meneso akambira a nambala five.
Project ya CARE yachitika zaka four zimene? Yabweretsako vuto lilose pakhomo la munthu kapena kumudzi kuno kwa Nsangwa? Koma kuthetsa mavuto ena. Koma kuthetsa mwatero number one? Eya, kuthetsako mavuto. Number three mfuna kuvomekeza a number one zomwe anena kuti kalero kudakalibe CARE tinali anthu aja oti ngati atinjata nsaka osadziwa komwe tulowera komano CARE itabwera indeno mavuto yali apo koma zina mwa izo zimene zimakhala ngati zimativuta panpa zayamba kuyendako. Zayamba kuyenda? Eya ndudziwa kuti pali ena mwina abweraso kudzatithandiza kuti kudzapitirize pamene CARE iyimire kaya idzipitiriza ndithundiye kuti tili bwino ndithu. Mwina ndipereke chitsanzo eti? Kuti mulinve nfunsolo likuta bwanji? Aah mkutheka kuti project ya CARE nthawi zina zake imakhala kuti yapereka mphanvu kwa azimayi eti? Eya . kukhala ngati kuti kuwamasula pakhomo ndiye pamatha kumabwera mavuto mabanja tsopano chifukwa cha nkhani ngati ziti? Izo. Ndiye Ndimafuna kufusa kuti project imeneyiyi sinathandizire kubweretsa vuto lina lilose pa moyo wamunthu? kapena kuno kwa Nswanga? Ngati mungakumbukire? Ine ndine number three, CARE, kabwera kwa CARE zomwe takamba kale kuti yatithandiza kwambiri chifukwa gender kapena kuti kadyedwe kabwino ndiye kuti zinthu zosezi zimayenda pamodzi. Ngati pali gender mukamayendetsa bwino gender ndiye kuti kadyedwe kabwinoso kayenera kayenda bwino. Kuyambira mbuyo tiyerekeze talima kandala komwe timapeza kanali kochepa, Kandalama komwe timapeza timangokagwiritsa ntchito abambo okha osawerenga kuti pakhomo tili ndi mkazi. Komano pozaphunzitsidwa monga ngati za gender kuchokera ku CARE ndiye kuti tidayamba kuti tikapeza ka ndalama kaya ka fafandende ndekuti amayi kodi chomwe mulibe muno mchiyani, ndiye pamafunika zakuti, ndiye kuti kusonyeza kuti CARE yatithandiza kuti mabanjamu zinthu zizyenda bwino. Eeh number two, number two ndukavomekeza kuti CARE, CARE chiyambire kugwira ntchito yake yatitandia kwambiri kukhala ozindikira zinthu zimene zoti kale sitimazindikira, chifukwa kale timangudalira kuti akati banja ndi kuti wamkulu ndi mamuna koma pano ndekuti zose tuyendera pamodzi kukonza budget titapeza ndalama, moti katundu yese wapakhomo timayendetsera limodzi ni mayi sitikhala so ndi gawo lonena kuti chinthu ichi ndi changa changa yayi. Timakonza budget titapeza ndalama pachaka kuti nde tichite chani tidya chani kuti pa nthawi imeneyi timakhala oti zimene tukonza kapena ndalamayi yimene tigwiritsire ntchito tukonzera pamodzi ndi mayi uja kale timangochita kuti tayipeza chili chose ndiye kuti uyenera kuimirirapo ndiwe bamboo osafusa ujeni maganizo kwa mzimayi. Koma pano timati tikapeza ndalama timakhala pansi tikonza budget tione kuti kodi chaka chinochi tiyendetsa bwanji, ndiye kuti zimezo zatitandiza kuti zinthu ziziyendamo bwino kusiyana ndikale komaso zizu tipatsa mavuto chifukwa zimayi onvetseta salutengaso gawo loti azyole mamuna chifukwa chonena kuti wampatsa ufulu oti iyeyo tichangamire limodzi za ndalama ija. Chifukwa pali ena amakhala kuti ukangoti takonzani budget kodi titani? Mwina amadzibakira kuti ndalama tapeza chaka chino ndikhoza kuvala zedi ndine , kapena mene mulimu chitani zakuti zakuti koma timakhla kuti tutani ,Panopa tazindikira kuti tikakhala ponzimodzi tukakonza zinthu tupereka maganizo mofanana, aah koma pakhomo pano chiluvuta, chavuta nchakuti chakuti nde timayamba mavuto wo kukonza ndiye kuti ndalama yotsarirayo yoti munthu akavaleko pamakhjala pambuyo ,kusiyana ndi kale kumangothamagira kukavala kusiya mavuto yomwe yali pakhomo. Chabwino tiyeni tipite patsogolo, tufuna tilowe gawo lina, gawo liemeneli takhala tikumalemba pa pepala ili eti? Tidzilemba zinthu pamenepo ndifotokoza kuti tilemba zotani.
Koma aliyese akhala akumaona zimene tikulemba. Tukufuna mutifotokozere inuyo azibambo akwa Nsangwa kuti kodi ntchito zochitka zomwe bamboo amakhala akuchita patsiku lake zimakhala ziti? Ndipo zimene amachita mzimayi patsiku lake zimakhala ziti? Ndiyekuti titha kuyamba ndi abambo, tiyambira azibambo eti kenaka timalizira ndani? A zimayi. Tiligawa tsiku lathu kuyambira mawa, masana kufika madzulo, mudzitiuza inuyo kuti kodi bamboo kukacha mamawa amatani? Tunvana eti? Ndiye ndufuna kuti ndichiyike pansipa ichichi ndikamalemba kapena chikhoza kukhala mene ndachinyamuliramu chifukwa inu mundiona apapa eti? Ndiye tiyambira , tiyambire abambo eti? Chabwino. Tipange chonchi koma, tugawa pakati uku kukhala kwa abambo uku kwa amayi eti? Ndiye tichite motero uku tidziyika nthawi, ndekuti apa tiyika zimene zochitika eti so apa ndikulemba kuti abambo, pamwambapa eti? Aha. Azibambo kunoko kwa Nsangwa amadzuka nthawi zanji mamawa? Nambala fili azibambo kuno kwa a Nswangwa amayenera kudzuka five koloko yeni yeni. Chabwino. Tose tuvomera kuti ndi five koloko eti? Timadzuka five? Faifi koloko mawa mwadzuka mumapanga zotani? Ine ndine number one monga nthawi ya season yolima five koloko mawa timalawirira kumunda Kulima. kulima kumeke kumunda waukulu kapena kudimba kapena zose? Zose , kudimba, kumunda. Chabwino kumeneko kumakhala kukalima basi? Kulibeso zina zimene makachita mukapita kumunda? Nchito zimene timapanga ngati a bambo? Number six pakali pano tili munthawi ya malimidwe a fodya ukhoza kudzuka mamawa, five kololoko kukchotsa nsakasi kumunda kuja. Chabwino. Kukathena fodya, chabwino, umakhala mamawa. Chabwino. Aaah kumunda kulibe zina zimene timachita zosiyana ndi za ulimi? Nambala fili, mmm ziliko zimene timachita koma zosemphana ndi za ulimi. Kumundako mwina zikhoza kutheka kuti munthawi ino tunena yochotsa sakasi, ukachotsa sakasi watopa ufuna kumabwerera kuno kunyumba ndeno umakhala ndi nthawi zomwe zija taphunzitsidwa ndi CARE mwina kutengako tinkhuni, tindiwo kumene, mayi kunyumba akalandire anga abu kupita nawo. Kutenga nkhuni? aahh , kupeza ndiwo? Chabwino. China nkhani chimene titha kukachita kumunda? Timakalima eti? Kulimako kutha kuimira zinthu zambirimbiri, kenaka kumakhala kutolera nkhuni kaya kupeza nkhuni kaya kuwaza koma mumabwera ndi nkhuni. Eya , kenena mukapeza ndiwo kaya zikakhala zokagula komko kaya zotolera pena pake eti, paliso china chimene machita kumunda kupatula po zimenezi? Apo ndekuti wakwana watheka ulendo obwera kuno kumudzi. Ndiye mabwera nthawi zanji? Kuweruka, ngati kuno kumudzi kuweruka sikuona nthawi ndi mene wathysapira ndime kumundako. Tiyeni tigwirizane ngati azibambo anthu ambiri amaweruka nthawi zanji kumundako? Ine nambala fili, ten koloko. Ten kokolo mubwera?
| 0 | 30 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_221.wav | 30 | 60 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_222.wav | 60 | 90 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_223.wav | 90 | 120 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_224.wav | 120 | 150 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_225.wav | 150 | 180 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_226.wav | 180 | 210 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_227.wav | 210 | 240 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_228.wav | 240 | 270 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_229.wav | 270 | 300 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_230.wav | 300 | 330 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_231.wav | 330 | 360 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_232.wav | 360 | 390 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_233.wav | 390 | 420 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_234.wav | 420 | 450 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_235.wav | 450 | 480 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_236.wav | 480 | 510 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_237.wav | 510 | 540 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_238.wav | 540 | 570 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_239.wav | 570 | 600 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_240.wav | 600 | 630 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_241.wav | 630 | 660 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_242.wav | 660 | 690 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_243.wav | 690 | 720 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_244.wav | 720 | 750 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_245.wav | 750 | 780 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_246.wav | 780 | 810 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_247.wav | 810 | 840 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_248.wav | 840 | 870 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_249.wav | 870 | 900 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_250.wav | 900 | 930 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_251.wav | 930 | 960 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_252.wav | 960 | 990 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_253.wav | 990 | 1,020 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_254.wav | 1,020 | 1,050 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_255.wav | 1,050 | 1,080 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_256.wav | 1,080 | 1,110 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_257.wav | 1,110 | 1,140 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_258.wav | 1,140 | 1,170 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_259.wav | 1,170 | 1,200 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_260.wav | 1,200 | 1,230 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_261.wav | 1,230 | 1,260 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_262.wav | 1,260 | 1,290 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_263.wav | 1,290 | 1,320 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_264.wav | 1,320 | 1,350 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_265.wav | 1,350 | 1,380 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_266.wav | 1,380 | 1,410 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_267.wav | 1,410 | 1,440 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_268.wav | 1,440 | 1,470 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_269.wav | 1,470 | 1,500 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_270.wav | 1,500 | 1,530 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_271.wav | 1,530 | 1,560 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_272.wav | 1,560 | 1,590 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_273.wav | 1,590 | 1,620 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_274.wav | 1,620 | 1,650 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_275.wav | 1,650 | 1,680 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_276.wav | 1,680 | 1,710 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_277.wav | 1,710 | 1,740 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_278.wav | 1,740 | 1,770 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_279.wav | 1,770 | 1,800 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_280.wav | 1,800 | 1,830 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_281.wav | 1,830 | 1,831.124188 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_282.wav | Choyamba ndifuse nawo kuti mwakhala mukutengapo mbali pa project ya chitukuko cha Sani? Pa chitukuko cha? Kapena ndifuseso? Kodi mwakhala mukutengapo mbali pa project ya chitukuko cha sani? Eye timatengapo mbali. Ndi ntchito ziti zomwe mwakhala mukutenga nawo mbali? Ntchito zolima chimanga, zolima fodya, swawa. Nambala chani inuyo? Five, oho nanga ena pa zomwe takhala tikutenga nawo mbali? Timalima soya, mpaka mene wuonjezera mene alikukambira iwowa. Ena? Kadyedwe kabwinotu, oho ena? Mene akukambira azangawa madyedwe abwino zimafunika kugwiritsira ntchito ndithu kuti upeze mtendere. Kulimapo swawa, soya mbatata eya. Ndithu. Mongokumbutsana tidzitchula manambala athu pakufuna kuyankha mafusowa owo eya ndine nambala chani? Four eti? Kodi tikamati kadyedwe kabwino timathandauza chani? Kadyedwe kabwino mkonena kuti muziphika zosamalika, peza kale makolo amati wana akakhala mpakati mazira asamadye ndekuti akhala ndi mwana otani? Ometeka tsitsi nde zimene zija nzakale koma tsano takhala ndi zamasiku ano. Ana akumadya mazira akakhala mpakati. Oho ndinu a namabala chani? Number six. Ine ndine number 3 pakhomo padzikhala kitchen chimbudzi ndi bafa ndiye kuti posamalika, ndiye pokhala kuphikira za ukhondo zija ana amasangalala pamen kuti ukawaphikire koma chimbudzi palibe ndiya ana aja amasowa koti apite ndiye umaoneka kuti khomo lija si khomo loyenerezeka. Khomo limayenera kukhala lovomere zeka padzikhala chimbudzicho kitchen mpogona. Nde wana uja ukamawaphikira thereÕre lija angakhale nkhwani ukamawahpikira nsima kuwapatsa amasangalala chifukwa akadya chakudya chija amathamagira kuti? Kuchimbudzi, ndiwo makhalidwe wawana. Ndiye ukatero pakhomo pamakhala posamalika popanda zina zilizose eya nambala five ahha. Nanga ena?
Mene nduneneramu nambala 4, ayi mpofunika ndithu , mene muno mutere atati amuleke leke muno mukhoza kuipa koma koma poti muli munthu mukhoza kukhala mopanda, ku kitcheniso chimodzi modzi nde zimayendera pamodzi. Mongowonjezera madyedwe abwino timanenaso monga kudya zamagulu, maganizo omwe timapanga pogula kaya pogulitsa kaya pokonza kaya posungaso chakudya, kulimaso monga mene mwanenera, kuyamwitsa kupita kuchipatala ukhondo wamadzi komaso kutengapo mbali kwa abambo kuzochitika za pakhomo. Kodi pali kusintha kukonse komwe kwachitika pa zaka zitatu zapitazi pa nkhani imeneyi ya madyedwe oyenera komaso maudindo amayi ndi abambo? Eya kudasintha number 3, kusintha kuli motere zaka zipita kumbuyoku ntchito zimathyola azimayi okha koma lero bamboo ndi mayi tikugwira mofanana oho. Eya, ena? Nambala folo, nambala 2, ndukhalira ndemanga mau akamba azangawa chifukwa kumbuyoku udindo munalibe. mzimayi mwina atha kukhala oyembekezera koma makasu athyoleko ndiwo, munthu wamkwazi atenge nkhuni makasu ali pa mbalipa oyembekezeraso mwanaso wina alikumbuyo.koma lero tupatsana udindo, obambo alikutengako mbali mwina ine nditha kuthyolako ndiwo koma thulo landio lija alunilanda akutengapo, makasu aja ali ulanda mwina ine nditha kwanguseza nkhuni zokha kumapita kunya. Mwina mtakafika nyumba kuja kuti mtengo tsuko nipite kudambo abambo ali kusadzulako tindiwo tija. Number 2 mene zasinthira kusiyana ndi mbuyomu sintha kwake mkwakuti kale kale wana, wazimayi amapita ku tchire kukapanga chimbudzi kapena nditi kukabiba ku tchire ndiye Panopa zinangoti zimenezizi zabwera kuno kwathu ayi zisinthu zidasintha. Oloko mwana wa zaka ziwiri zitatu amapita kuchimbudzi ndiye kuchimbudzi kwathuso tidayikako kasamba manja. Akatha kubiba amasamba manja mkumapita kunyumba kumakasewera pamodzi ndi azizake, ndiye mwana ujaso timamupatsa kunyumbako asanafikeso po azizake paja mwina tiyikepo madzi athu akuti mwana uja amayenera asamba mumupatse zovala zabwino akhala pa gulu pa anzake. Ndiyetuona kuti maganizo abwino adabwerawa zinthu zidasinthaa kwathu kuno ndithu tuwona kuti ukhondo ukuchitika ndithu mudzi mwathu muno, pakhomo pathu timayeneraso kusetsa tsiku lililose tisanapite kumunda pobwera kumunda kuja timadzapeza kuti ayi pakhomo paja pali bwino. Mwana ujaso akamachoka kodya misinde amakataya kutchire podziwa kuti amama asamala kale, ndiye Panopa tili ndi moyo wabwino, ngakhale njala ili pakati koma aha zina zina tikuona kuti zinthu zili bwino ndithu. Koma bungwe lake ndi la CARE li lidatithandiza zedi. Number six motiso tikambepo kuti yayi zimenezi zidasintha chifukwa masiku akalewo titayamba kuti tupita kumunda timatchyoka wapansi kutenga khasu, lodala tatenga ndekuti lathu tatenga ndiye uku mwana tabereka kumbuyo ndiye timalema koma kujako talima timawerengerana mizere ndiye kuti itatutu itatu tilimandithu koma pobwera kuthyokaso ndi nkhuni makasu aja mwana kumbuyo ndiye timathyoka nayo. Kabwera kumudzi titenga tsuko uja kupita ku dambo kukatunga madzi kujigo, titabwerako tiyambe kudzula ndiwo zija tiphike tiphike nsima, kuphikitsa madzi amuna, amuna aja amangukhala ali phe koma tsanu lero, ayi zidasintha amunawo amapsyedako nyumba mpyephye ndiye kuti iweyo ukupita kudambo kujigo. Lero zidasintha mwina tere kuphikako ka nsima ndiye kuti ayi tere uona kuti zinthu zasintha ndithu.
Mwanena mau okuti kupsyeda? Eya kusesa, eya oho Zikomo. Kusesa pakhomo, nyumba hahahah ahh. A number four, nambala mawu ake nawomwewa tere wanena nzangayu. mau ake niomwewa wanena nzangayu. kuti chitukuko chiliko ndithu. Nanga zomwe sizinasinthe pa zaka zitatu zimene zi ndi chani? Koma zosasintha nambala five ahh situzipenyaaah kweni kweni chifukwa kutengera mene udaliri moyo wakale ndi watsano udasintha zedi. Ukapeza mwana kumpenya litsiro ali naka naka pali anthu ake. Koma ana amasiku ano akangusamba komatu mwana ochepa koma ukampeza ali kakala kala kwama ndalero lero la chani? Lachiwiri. Aah mwanatu wanthete tu amakeso ah palije tsiku loti wangugona osasamba koma tsiku lilose alisamba ndiye timati bukhondo ndi uti? Umenewu chifukwa ngati munthu asamalira chiwiya chanyumba ndiye kuti zose amatani amasamala eya. Tsono ukhondo wa lero aaah tusiyanista ndi umo tidabadwira ife masiku awo ndi lero li, eya ndithu. Ndimavuto otani omwe inu kapena ena akukumana nawobe pa zamadyedwe oyenera makomo kapena midzi? Number three, mavuto amadyedwe abwino omwe akukumana nawo ndiwo adati ine ndikhokhala chete, koma yemwe alikugwira gwira sangakumane nawo chifukwa pa nkhani ya chakudya chani chino chavutadi zedi koma bodza CARE yi idatiuza chifukwa idtiuza machitidwe oti tidzitani kodi? Tidzithandizidwa tilimepo timbatata, timbatatesi tili kudya titi timeneto. Number one CARE yomweyi mwina anabwera mu august ka sptember anati musamadalire zinthu zongulandira, zongulandira mudzafa ndinjala zizakuvutani ndiye pali npano aliyese pakhomo pake akonze dimba ndiye panali madongosolo moti tabyalamo ndithu, ndiwo sitidaguleko timbatata tidatani tidadya ndithu. Panopa ka dowe ndithu timadya ka makomo mwathumu. Titaona kuwi owoo ndiye kuti mbungwe la CARE likubweretsa zinanazi zoti tidzidzala makomo ndiye kuti malangizo ena atabwera tidzizati tidakoza kale pakhomo pathu.
Kodi project imeneyi ya Sun yabweretsako mavuto ena aliwonse? Mavuto ma pathupi pamunthu kapena pamodzi Panopa sangalephere amakhalapo ndithu eya chifukwa ngati munthu anabadwa pa dziko la pansi anabadwira vuto komaso mtendere, chifukwa sungangokhala kose kwabwino munthu aaah kwina kumakhala kopendekera ndithu ngakhale akhala ochita bwino cha mtundu wanji uwona apita pakhomo pa mphawi ngati ine ayi mutandibwerekako mchaku aah chukuti kodi ah poti nali nacho pangÕono kwayakoni pangÕono nde timampatsa munthu uja akakakonza ku nyumba kwakweko ndiye kuti amakhala kuti waombokerako pa chinthu chimene chijacho eya, ndithu. Ena ali ndi maganizo ena? Number two ndemanga monga ali kukambira amayi awa kuti vuto masiku amenewo kusanabwere CARE yu timavutika zedi chifukwa nanga sinaga panalibe langizi otiphunzitsa mene tingagwirire ntchito koma mene anati wabwer CARE mu alangizi alugwira ntchito ngati wa Sandram mau adakamba amayi awo okuti mwezi uwowo anatiuza tilime madimba tinalimadi madimbabo moti mwezi uwowo sitidagule ndiwo, aah ngati mwezi uwo tagula ndiwo? Angakhale mondokwawo tayamba pakanthawi ndithu moti tingokulandirana ndi waku mundawu ndi waku dimbawu, madimba apakhomo. Ndiye kuti apapa tikunena zakuti project imene yiyi ya CARE sinabweretse mavuto ena aliwose koma no mavutowo ndi okhazikika ndikale? Mavuto a project ya CARE sidabweretseko ayi. Panopa ndi nthawi yoti tikambirane za ka gawidwe ka ntchito mungatenge tsiku lathu mene timachitira kuyambira mawa mpaka madzulo mene timakagona, komano kagawidwe ka ntchito kameneka ndi ka amayi ndi abambo omwe ali ndi ana angoÕno angÕono osapyola zaka zisanu.
Kumbali ya abambo amene ali ndi ana angÕono angÕono amene ali wosachepera zaka zisanu ndi nthawi yanji yomwe iwo amadzuka? Kumbali ya ana ngÕono angÕono mwina ena amauka mamawa uja mene amakhalira ana amasiku anowa. Ena mwina amauka uyeni uyu 7 koloko 8 koloko walikukhala chogona malingana ndi zamasiku ano umati aah mwana ameneyu agalamuka niyesa wachita malungo koma pamne mwina mwana alupeza bwino ndiye tulo tapitirira ndithu ndiye uja amadzutsa mwana uja kupita naye pakhomo kuti kodi iwe lero watani usakudzuka nsanga. Ndiye mwana uja amauka kumpenya thupi lozizira eya. Nanga kumbali aa ndingonena kuti abambo, mbali ya abambo omwe ali ndi ana ngÕongo angÕono ndi nthawi iti yomwe amadzuka abambowo? Amadzuka mamawa, amadzuka mamawa, akadzuka mamawa mwina amayi aja alinyumba ndiye kuti abambo aja akadzuka mamawa amatenga chiseso kumasesa pakhomo. Imakhala kuti mamawa wake ndi nthawi zanji? Mwina ngati six koloko. Nde akadzuka akasesa panja china chomwe amachita ndi chani? Mwina momwe nimaonera ineyo mwina ajawa akauka akasesa sesa pakhomo paja nde ngati pali maungu npakhomo amatenga maungu aja kumwanya mwanya basi mkuphika kuti mawa kutacha wana aja akadzuka adye popita ku church pakakhala kuti mpasabata. Oho nanga ena? Number one mwana osachepera zaka five nose ni makhala busy ndi wana waja , sinanga mwina poti tusunga adzukulu eh woo wathu ndiye adatha nde timakhala ni busy tose kapena kuti tose ndi wa muna tusunga adzukulu aja, ena ali ndi amayi okha abambo adapita ena ali ndi abambo okha amayi anapita ndiye . koma mukakhala kuti muli nose mumakhala ni busy ndi adzukuluwo aja kukacha nanawa umamuona ndithu kuti mwana asamalike monga ngati ineyo mzimayi ni mauka mamawa uja ndikasesa sesa pakhomo ndikasesa kitchen kuikapo timadzi basi ndi sambitse adzukulu aja ngati kuli mkaka kaschool ka mkaka basi niwanyamule nipite nawo kuja ndiye kuti kunyumbaku mapatsaso kanthu kopita nako ku school. Nanga tikachoka poti abambo amatha kuphika chakudya kaya ndi maungu amenewa akamaliza zimenezo amapanga chani? A number two, mkachokapo ine mkasiyapo abambowo amakhala ndi busy yoyangÕanira mwana uja maka maka ine popeza ndili ndi mwana wa matenda ndimawasira udindo waukulu pakhomo mtachoka ine wama yangÕanira kwabasi koma ndi tsikana amaphitsa madzi mkuwuza munthu kuti popeza ineyo amake amwana uyu achokapo munitsukireko. Ndiye amati munthuyo akabwera amantenga mkukatsuka basi ndikukhazika ndiye kuti iwowo ali busy zoyangÕana chani chakudya kuti aphike mwana uja adye. Ine nili kwina numo amachitira. Nthawi yomwe amapita kukayangÕana chakudyacho ndi nthawi yanji? Ingakhale nthawi yanji? Nthawi yomwe amakayanganira chakudya mwina ma eight koloko akayanga chakudya ngati atangwanika ndi ntchito ina pakhomopo mwina apita ma ten koloko ali wuyangÕana chakudyacho. Oho nanga ena? bamboo amadzuka mamawa amati atadzuka amasesa pakhomo mkuesa mu kitchen kutereka madzi kuti mwana uja akadzuka asambe maso. Ndipo akamusambitsa maso ngati kuli kusamba maso mwana uja akakhala bamboo odzichitani amati waikapo kaphala mkuphika ka phala kaja mkupatsa mwana uja. Ndekuti pamene udzuke iwe mayi wake ndiye kuti bamboo zina wachitapo kale. Ndekuti Ntchito zimakhala zothandizana? eyaa. Akachoka pamenepo china chomwe amapanga ndi chani? Akachoka pamenepo akakhala bamboo ozichitani zomwe zija ndanena kuti poti kuli gender masiku ano nde kuti ngati palibe nkhuni pakhomo bamboyo akuti tiye kumunda tikawaze nkhuni muchoka kuja ndiye kuti iye wasenzako nkhuni ine ndekuti ndatengakoso chani? Ndiwo manja kapena ine ndatenga ndiwo manja ndiye kuti pamene ine ndidzikoleza moto iwo alikusadzulako ndiwo zija. Akasadzula ndiwo zija ndiye kuti ine ndipita kudambo ndiye kuti madzi dzathira nipita njira yachiwiri ndiye kuti ndidzapeza madzi wateleka pamoto kuti ayikepo ndiwo zija. Imakhala nthawi yanji imeneyi? Iyenera kukhala leven sinanga timaleka 12 kuti wana wadye. Mkamaliza kudyamo mpaka madya mumakonza zakudya 12 mpaka ma 1? Aha , I mean ma 11 mpaka ma 12 eya, tikupanga leven ija kuphika ndiwo ndiye kuti chama 12 tiphika nsima yake ndiye kuti pamen tiphula nsima titereke madzi abambo aja asambe, ngati alimkoyenda akayende ife tipitilize za pakhomo. Ndiye ngati kuli za ntchito tipitilize zakumunda zose tikabwera uko tidzapange za pakhomo. Nde abambo amatha kupita koyenda umakhala masana amenewo? Masana . imakhala nthawi zanji? Monga Panopa cha ma 2 koloko amapita ku mpira kwa azawo akachita kusangulutsako pangono adzanipeza ine zapakhomo namaliza, ndiye amati poti iwe unagwirapo ndiye kuti za madzulo ndiphika ndine. Nde akaphikano madzulowo china amachita ndi chani? Enaso mutha kumayankha ahahahah, tsano nthawi yamadzulo imakhala yopumula, munthu uja amakhala akudikira kuti adye akapumule pamphasa agone. Ndiye kuti mawa muja mene mwapenya kwathu kuno adzikagwira ntchito ya fodya kumunda. Akakagwira ntchito ya fodya ija ndi nthawi yoti munthu wa mkazi achoka kumunda kuja atengekoso zakudya zokadya zamasana. Zamawa zija zama leveni koloko. Akadya zimene zija ndiye kuti ali nthawi yoti athyole fodya azisoka ndiye akakhala pa nthawi imeneyi munthu wamuna ali kugwira ndinthu munthu wamkaziyo apite kunyumba akaphika ndiwo kunyumba akaphika nsima tikadye tikagwire ntchito ya fodya. Tikatha ntchito ya fodya ija basi uyo adzitakata nianmweyo kuti ah tsopanapezako ufuko ufulu ntchito yachapa. Nthawi yopitira kumunda wafodya yu mumakhalaso ma six momwemo? Ayi mumakhala ma seven koloko timadziwa kuti fodya uja wapiti mphepo mame aja aphwa ndiye udzipita kumunda ma seven koloko paja ukathyole fodya uzichoka kumene kuja mwina izikhala ma ten koloko mwina ma 11 ndiye ukabwerako uliso ndi ntchito ya pakhomopo kuti upitirize ntchito ya pakhomo ntchito ya kudya sikutha ndithu. Ngati imatha ngati? Malire ake udzathe moyo hahaha.ukadzatha moyo uja ndiye umadzati ntchito ya kudya ndaitani? Ndaileka zedi ndithudi tere mmm. Ndiye kumadzuloku amagona nthawi zanji?
Kugona ndiye aa amagona ma seven mauyeni ma seven koloko ena amakhala kucheza zedi ena amagona ma eight koloko ena ma ten, mbali zakwathu amagona ma 9 koloko. 7 ndithu magona ine. Ndithutu ma 8 ma 7 koloko nthawi yoti munthu watani kodi? Watha kudya, kumagona. Enaso amatangwanika zokamba, ndithu. Nanga kumbnali ya amayi amene ali ndi ana angÕono angÕono osapyola zaka zisanu amenewa amadzuka nthawi yanji? Ama banja mwao? Amabanja mwao enatu amauka mamawa six koloko ija ulendo kubwalo akakasesa sesa kubwalo kuja akakatha zija anena kale akaike madzi asamale mwana maso, chifukwatu mwana umafunika kunsambitsa ndithu sinanga amakhala nyango, nde ana aja ukawatsuka tsuka ndiye ukakhala udawazolowetsa kudya mamawa ndiye amaikapo phala. Amawo aja phala ija pha pha mwana aliyese adye ndiye ngati chili gaige chije ndiye kuti amwetsa mwetsa phala lija tuwana tija tukasewera. Ndiye kuti nyengo ina zomwe tikamba kale za fodya zi alupezeka alusiya mwana uja ulendo wotani opita kumunda Akaka thyola thyola fodya uja akabwerako ndi wana angono angonowo amapezeka kuti akutani ayikepo madzi asambike kuti apeze bwino chifukwa akangomuleka amakhala kalira. Chifukwa kumunda kuja zinthu zija zuyabwa yabwa thupi. Eeh niyesa mwana uyu njala aphike phala amwetsa ali kukagwiraso ntchito zija yoti adye akaphika phika nkhwani iye alikudya thothi, akangosadzula sadzula kukalula akangokudya ali kutani pa ticket ya fodya . nthawi yanji imeneyi? Pamenepopo ili ma 12, ili ma 1, ma 1 koloko ambiritu amakonda kudya ma 1 sinanga atangwanika ndithudi. Zikomo, ndithu. Nanga ena? Momwmo ndithu tere kuti amadzuka mamawa akadzuka mawa anawo ngati enawo ali opita ku school ndiye amati akadzuka mkupita kitchen mkusesasesa kuwola phulusa wawo kukataya mkusonkha moto, kuikapo madzi kukhazika muja ana aja alikukasamba ndekuti wana aja wali kuwayikirapo phala lija mkuphika tee nde wana aja kumamwa adzipita ku school. Ndekuti uja wangÕono uju kodi agogo muchokapo ayi tee sinduchokapo basi ali uyutu mwana, nde ife mwana uja ife tupita kumunda tukathyola fodya ndekuti ife tidikira wangÕono uja takhala naye ndife. Kuja kuti wana aja apita ku school akabwera kuja wana waja visongole vili kuti ndiye kuti ayamba kusoka fodya ndiye kuti ife tsano kamwana kaja katitayaso kathamangira amayi ake abwera kumunda. Amabwera nthawi zaji kumundako? Amabwera leven koloko, leven koloko? Eya ndiye akabwera kumundako china chomwe amachita ndi chani? Amati akabwerako basi kupita ku dambo kukatunga madzi ku jigo. Ndikuphika ndiye kuti ifeyo tusokako fodya uja. Akaphika nsima mkuphika ndiwo tikudya nsima ija. Ndipo tsano kumatani? Kumagwira chisongolo aposo ndekuti uku madzi ayikapo kuti tikatha ntchito iyi asambe. Kusamba kumakhala nthawi zanji? Malinga akangotha ntchito ija kusoka ndikupakira oho. Muganiza ikha khale nthawi zanji? Cha ma 4? Olo madzulo chifukwa imakhala ntchito zedi. Ndiye akamaliza kusambamo china amachita ndi chani? Amapita ko Kayembe kukayenda.
| 0 | 30 |
./data/chichewa-dataset\audio\segment_283.wav | 30 | 60 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_284.wav | 60 | 90 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_285.wav | 90 | 120 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_286.wav | 120 | 150 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_287.wav | 150 | 180 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_288.wav | 180 | 210 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_289.wav | 210 | 240 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_290.wav | 240 | 270 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_291.wav | 270 | 300 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_292.wav | 300 | 330 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_293.wav | 330 | 360 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_294.wav | 360 | 390 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_295.wav | 390 | 420 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_296.wav | 420 | 450 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_297.wav | 450 | 480 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_298.wav | 480 | 510 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_299.wav | 510 | 540 |
|
./data/chichewa-dataset\audio\segment_300.wav | 540 | 570 |