audio
stringlengths
43
45
text
stringlengths
0
24.1k
start_time
int64
0
1.83k
end_time
float64
1.74
1.85k
./data/chichewa-dataset\audio\segment_401.wav
1,740
1,770
./data/chichewa-dataset\audio\segment_402.wav
1,770
1,799.823688
./data/chichewa-dataset\audio\segment_403.wav
Aaaa tili kuno mmudzi wa Msangwa, a Group a Msangwa, TA kayembe, kuzacheza ndi A tsogoleri amene akugwira nawo ntchito ndi a bungwe la Care. Muli ndi Udindo wanji mmudzi uno? Village Headman Msangwa. Chabwino. Inu ngati Village Headman mumapanga zotani? Aaa Village Headman Msangwa, Mmmh. Ntchito zanga nkuyangÕanira anthu mmudzi. Chabwino. Aaa Kodi mwakhala mukutengapo mbali pa Project ya Care, imene imachitika kuno? Eeee ndimatengapo mbali. Mwatengapo mbali mmagawo wotani? Magawo yowaunikila anthu aja pa zakufunikila Kwa Care. Chabwino.Mukati mmaaunikila mmawauza zotani? Ndimawauza kunena kuti bungwe la Care, lofunika zimene lanena tiyeni tizitsatire. Chabwino. Zimene bungwelo laphunzitsa Mmm Tiyenela kuzitsatira Kuwaziwitsa anthu aja kuwauza kuwapatsa chilimbikitso. Chabwino chabwino. Eeee. Ndi zina ziti zimene mumachita nawo ndi a Care ngati mfumu? Wa Care, ndiye kuti Pali ntchito monga, kukhala nti madimba zimene a Care adatiphunzitsa, madyebwe abwino. Mmmh. Ndiye kuti ukhondo, Mmmmh. Wofunika pakati pathu, ndiye kuti zimenezo zutheka chifukwa cha Wa Care. Chabwino. Mukanena za timadimba tapakhomo, amanena kuti chani kapena mmatani? Timadimba tamÕmakomo timeneti timalima kaya kuseli Kwa nyumba, Mmm Tibzalamo tindiwo tofunikira kuti tisamasoweke ndiwo pakhomo pathu. Chabwino. Timadimba toyerekezela tapakhomo. Chabwino. Eee Kumbali ya kadyedwe kabwino mwaphunzitidwa zotani? Kumbali ya kadyedwe kabwino ndiye kuti pali ndiwo zamasamba, tidzidya zinthu zosinthasintha. Zosinthasintha. Eee timasamba, Tochokeza monga kaya zipatso. Mmm Kadibwe kabwinoko kali mmenemo.Kumachita zinthu zosinthasintha monga kumadibwe zizikhala zosinthasintha, tizakudya tofunikira ndithu pakati pathupi la munthu koma zudzera mÕbungwe la Care. Kumbali ya Ukhondo mwaphunzira zotani? Kumbali ya Ukhondo, kukhala ndi zimbuzi, kulambula mmakomo,makomo akhale mudzikhala molambula,ndipo tikhale ndi bafa, ndizinthu zambiri zimene Care yatiphunzitsa kukhudzana ndi ukhondo. Chabwino.Ngati zina mungakumbukile mutifotokozela. TILOWE GAWO LINA LA MAFUNSO Ndi zinthu ziti zimene anthu a mÕdela lino amakhulupilira mokhudzana ndi udindo wa amayi ndi abambo pa kadyedwe kabwino? Kunoko kwa Msangwa anthu amakhulupilira zotani zikhulupiliro zawo pankhani ya kadyedwe kabwino molingana ndi maudindo a abambo ndi amayi? Aaa kuno amakhulupilira, kadibwe kabwino pakati pa amayi ni abambo, powa pa mgwirizano pa banjapo. Ndiye mukagwirizana pa banjapo, mumakhalilana pansi kuti ndiye kuti tidzidya bwino tiyenela kutani, ndiye mukakhalilana pansi pakati pa bambo ndi mayi, ndiye mmaona chochitika choti zinthuzo monga kadyedwe kabwinoko, kapezeke. Chabwino. Eya Kutanthauza kuti pamafunika kuti pakhale kupangila limodzi ziganizo? Eya, kupangira limodzi chiganizo kuti kodi kuti tidye bwino, kuti tichite izi kuti zitiyendele titani. Ndiye mmapatsa chiganizo anthu awiri mamuna ndi nkazi. Chabwino. Ndi zinthu ziti zimene mumaona kuti izizi nzimene zimayenela kukhala chonchi, kapena nzoyenela zimene mÕbambo akhonza kuchita pa nkhani ya madyedwe, kapena mÕmayi akhonza kuchita pa nkhani ya madyedwe? Mukhonza kupangana kuti pabanja pano zinthu zisamativute zija nnakamba kale, mukhonza kulima timadimba, kaya tikakwera kuntundaku chifukwa chakenso atiphunzitsanso ulimi mmuja nnanenela, atiphunzitsa ulimi tikakwera kuntundaku, tikhonza kulimako kaya ndi ntedza, kaya nsoya nchani, zimenezizi ndi zimene zoti amakhala madyebwe abwino pakati pamuthu, komanso ngakhale zipatso kumene nzofunikila kuti munthu mitengo ya zipatso azibzyala zimene zimathandiza kuti pakhomopo pasamakhala posowa kanthu. Eee, Kwenikweni chimene timafuna timve nkunena kuti kodi inuyo mumakhulupilira zitiziti tikamakamba pa nkhani ya madyedwe, zikhulupiliro zanu zakunoko ndi zotani? Zikhulupiliro zathu zakuno ndi kuchita zinthuzo mwa mÕgwirizano kuti tidzidya zinthu moyenelera.Kadyebwe kabwino ku mbali ya zikhulupiliro ife siti, timakhulupilira kuti zinthu zones zija tiyenela kuchita mosasiyana, madyebwe yosasiyana. Chabwino. Pakati pa mayi ndi bambo ngakhalensoa ana. Chabwino. Palibe kusankha kuti uyu ayenela kutere, ichi nchoyenela ana kapena mayi kapena bamboo, koma zimene zoyenela kudya tuyenela kudya mofanana. Chabwino. Eeee Mulibe miyambo ina iliyonse imene mumakhala nayo yokhudzana ndi kadyedwe? Aaaa pakati pa kadyebwe palibe mwambo wina. Chabwino. Ndiye izizi zimene inuyo mmakhulupilira, kodi nzimenenso mmachita? Chifukwa pali kukhulupilira ndiye pali kuchita.Zimene munana apapazi nzimene mumachita kuti kadyedwe mmadyanso chimodzimodzi? Kuti mmakambirana pankhani ya madyedwe pakati pa abambo ndi amayi? Eee nzimene timachita kukhalirana pansi kuti kodi zinthu kuti zitiyendele titani, ndiye mmakhala kupatsana ziganizo anthu awiri kuti pafunika titsate gawo ili kuti tipeze chakudya choyenelela, kuti madyebwe athu akhale abwino. Chabwino. Aaaa, ndiziti zimene zasintha mu zaka zimene Care yakhala ikugwira ntchito kunoko eti? Chabwino. Panali Zikhulupiliro zimene munali nazo kumbuyoku zimene panopa mwasiya kapena zikhulupiliro zimene munalibe zimene mwayamba chifukwa cha a Care? Pamene bungwe la a Care lafika, latiphunzitsa zinthu zambiri, Mmmm Pali kadyebwe kabwino kamene mmbuyomu sizimatsatidwa, wana amadyetsedwa chakudya moyenelela ngakhaleso ife akuluakulu timadya chakudya moyenelela koma kudzela mÕbungwe la a Care, Mmm kuchoka nkuphunzira muja ndanena kale kuti tili mmadimba, Mmm Ndipo tili ndi madzi yabwino, Mmm Koma kudzela mu Ulangizi wa Care. Mmm Eee nikhonza kukamba motero popeza zolankhula zimapita mwambiri mafunso, ndiye mwina sinnalondoloze mmene mungandifunsile koma kuchoka nthawi imeneyo ndiye kuti bungwe la Care labwela ndizinthu zambiri asintha chifukwa anthu tili athanzi chifukwa cha zakudya zoyenelela. Chabwino. Tinene chonchi, Mmm. A Care akubweretselani zikhulupiliro zotani pa nkhani ya madyedwe zimene inuyo poyamba simunkakhulupilira komanso simunkapanga. A Care? Mmm. Wa Care tidzinkamba pa mÕdzimodzi, zikhulupiliro zimene a Care atipatsa nkutilimbikitsa monga kukhala ndi madimba, ukhondo, zimenezozo zimapangitsa kuti munthuwe pakati pa zimenezi umakhalabe ukudya bwino koma zuchoka nkuphunzitsidwa ndi bungwe la Care. Chabwino. Mukakhala pakhomo panu inuyo,eti, Mmm Ndi ziti zimene mumachita kumbali ya kadyedwe zimene poyamba simunkachita? Mungotipatsa zitsanzo. Kumbali ya kadyebwe ndiye kuti timayesetsa kukonzekera chakudya, eeh kuti tisamakhale ovutikila nthawi yayitali, timalima kaya dimba kuti ndiwo zisamatisowe tisamavutika ndi zinthu zambiri, timalima mbatata, kuti pakhomopo tidziona chakudya choyenelela. Zimenezizi kaya nthawi zina tikagulapo kaya ntizipatso ngati tizipatsozo pakhomo pathu palibe, nzimene zutipangitsa kuti pakhomopo nkamatero mmaona kuti zikuyenda.Zija ndanena kale kuntunda, kuli nsawa ,soya,chimanga, zimene timazilingilira kuchoka mu upangiri wa Care,taphunzira kuti tiyenela pakhomo pathu pano, zoweta kukhala nzoweta pakhomo.Mmm Palinso zina zimene mmafuna kuonjezela,zimene mwanena kalezo? Zimene ndanena kalezi? Mmm Aaa zimene ndanena kalezi ndi momuja ndanenelakuti madyebwe abwino tawaphunzira pophunzitsidwa ndi a Care, ndiye kuti pakhomopo mayi ndi bamboo mmakhalilana pansi kuti kodi tiyenela kudya chakudya chotani mtsiku lalero, ndiye kuti zimene zijazo mwakhalirana pansi. Kaya mawa tiyenela kuchita chiyani, chifukwa nthawi zina chochita mawa mmachikonza ngati lero koma osati pawekha koma ngati banja, bamboo ndi mayi mukonze zofunikila kuti mudye, kuti banjalo lisavutike kumbali ya chakudya mwachidule titero. Chabwino. Tamphu tamudziwa chifukwa cha bungwe la Care ndipo zationetsa kuti tili nacho chikhulupikiro chonena kuti, tili mchikhulupiliro ku ana athu amene kaya anali onyentchela ali ndi ma tupi oyenelela chifukwa cha Ndisakanizeni. Tadziona nzofunikila kwambiri pa miyoyo yathu. Mukamati ndisakanizeni mutanthauza ndi chani kwenikweni? Ndisakanizeni? Mmm Tizakudya, tinthu tamagulu angapo. Mmm Zakudya za magulu angapo. Mmachita kugula kapena mmachita kupanga nokha, Ndisakanizeniyo? Pali Ndisakanizeni amene a bungwe la Care amapereka ku ana, kuti tiyambe kudziwa kuti pali Ndisakanizeni, liu loti Ndisakanizeni tidalidziwa kuchokera ku bungwe la Care zitabwera zofuna kupatsa,zopatsa wana oti ozidya. Ndiye pokhala pomwepo nkumaphunzira kuti kodi muti nchani, aah ameneyu ndisakanizeni amene akhulalila wana kuti odzikula mwa thanzi. Chabwino.Moti inuyo Ndisakanizeni mwamudziwa chifukwa cha Project ya Care? Eee Oh Sorry. Tamudziwa chifukwa cha Project ya Care. Chabwino. Ndiye anakuphunzitsani kapangidwe kake ka Ndisakanizeni kapena mumangolandirabe kuchokera ku Care? Kapangidwe kake, panopa nikhonza kuti, odalankhula ndithu, komabe nzotii, zandithawa. Zakuthawani? Eya kuti makonzedwe ake ni aka ni aka ni aka. Chabwino. Koma anaphunzitsa? Eeee Chabwino. TIYENI TILOWE GAWO LINA LAMAFUNSO ATHU ETI. Chabwino. Ndimafuna mundiuze zochitikachitika zikuluzikulu, mmudzi munomo, zimene zachitika mu nthawi imene Project ya Care yakhala ikuchitika kuno eti. Mmm Kuyambila chaka cha 2017, kufika tsiku la lero, pachitika zochitika zotani zikuluzikulu zokhudzana ndi madyedwe abwino kunoko, koma zochitikazo zisakhale zokhudzana ndi Care ah ah, zikhale kuti zimachitika koma osati mu Program ya Care? Kaya mundimvetsa kaya? Zochitika zosati zokhudzana ndi Care ayi? Ahaaa. Vuto limene tinakumana nalo, chaka chatha, ndi Mphuzi, zinaononga kwambiri mbewu. Mbuzi? Mphuziii. Mphuzi. Mphuzi ndi chani? Mphuzi ni tizilombo tima, timakhala ta maonekedwe oyera, timadzadya mizu kupansi, osati Kapuchi,aah koma ito timadyela kupansi. Chabwino. Timalimbana ndi mizu ya Mbewu ija, Chabwino. Pamene Kapuchi amalimbana mpamwamba, mbewu ija amaikuila pamwamba. Chabwino. Imeneyo ni, timati Mphunzi, kaya ili mÕdzina lina chabwino koma kuno kwathu imadziwika ndi dzina loti Mphuzi, zimene zinatisowetsa ntendere chaka chathachi. Chabwino. Aaa Mphuzi zimenezi zimalimbana kwambiri ndi mbewu iti? Mphuzi zimenezi zimalimbana ni chimanga, pamenepatu mpodontha. Tingotere. Chimanga, Soya, ngakhalenso Sawa. Chabwino. Eee Mphuzi zimenezo. AaaH sizidalimbanepo ndi zinthu zimene mmalima ntimadimba tingÕonotingÕono? Ntimadimba tingÕonotingÕono, Mphuzi zo sizidafike poti taziona kuti talimbana nazo monga nkulima kwathu kwa chaka chathachi, tinalima mmadimba angÕonoangÕonowa, koma MPhunzizo monga kwa ine sindidafike poti ndaziona kuti zafika poti zatigwira. Koma kumunda nkumene zidazatisautsa. Chabwino. Eeee. Ndi Zina ziti zikuluzikulu zimene mungakumbuke zimene zachitika kupatulako Mphuzizi? Zimene zachitika zikuluzikulu? Mmmm, MÕZaka zitatu zimenezi. Eee, chifukwa tikhonza kukumbukiranso kumbuyoku kuti njala inali pakati pathu, koma mchaka ii cha kumbuyoku. Mchaka chake chitichiti? Two and chani kodi imene ija? Njala inativuta koophya. 2018, 2019, 2017? Kodi imene ija 20 nchani kodi, 20É. Papita zaka zingati? Eee! Four zonse koma zilikukwana. Chabwino. Eee chabe popeza sitisungira kuti chaka chakuti tidavutika motere. Mmm Eee timangoti koma chaka chino chativuta monga mmene panopa zativutila, ndiye timante, tikatero ndiye kuti tisungire kuti chaka chakuti tinavutika motere, zija zimangokhala kuti taziiwala. Chabwino.Palibe chimene chachitikapo chokhudzana chabwino, Chabwino? Chokhudzana ndi madyedwe? Chabwino? Mmm. Nzaka zitatu zimene zapitazi? Madyedwe mzaka zitatu zapitazi, a Care, koma ndikumbuyo kwenikweni, a Care amatipatsa timati Likuni Phala, chifukwa zimenezo ziinabwera ndi bungwe la Care, Likuni Phala. Mmm. Ada, ngakhale chimanga, a bungwe la Care adaperekako. Chabwino. Ndimafuna ndimve ngati mudalandilako thandizo lotelo kuchokera ku mabungwe ena zaka zitatu zapitazo? Mabungwe ena adaperekako monga CICOD. CICOD? Eee. Anapereka chaka chiti? Aaah, chaka chatha icho, papita ngati si zaka zitatu apa. 2017? Yayenela kukhala choncho, ee CICOD idaperekapo. Adapereka chani? Chimanga. Chimanga.Kwa aliyense? Eeee Kapena kwa anthu osankhika? Eee, zimakhala, zimasankha anthu. Chabwino.Amasankha anthu otani? Osaukitsitsa. Chabwino. China nchani chimene mukhonza kukambapo cha madyedwe abwino chimene mwina munalandira ngati thandizo, zochitika mwina zabwino? Mathandizowo monga muja nnanenela kuti bungwe la Care ndiye lakhala litithandiza mu nthawi imeneyi, eee. Chasintha kwambiri mmudzi unowo pa nkhani ya madyedwe oyenela ndichani? Chimene mukhonza kuchifotokoza kuti chasintha kwambiri pa nkhani ya kadyedwe koyenela ndi chani? Anthu tukhala a thanzi. Athanzi. Mmm Thanzi labwera chifukwa chani? Thanzi labwera chifukwa chodya bwino kudzela mu bungwe la Care. Chabwino. Ndizipitilila? Thanzili labwera kuchoka mÕbungwe la Care,chifukwa chotiphunzitsa kulima zinthu zofunikila pa miyoyo yathu, monga ndiwo zamasamba zija ndanena, zipatso zija ndanena, ndiponso kukhalanso ndi ukhondonso nzimene zimapangitsanso kuti anthunu mukazi mukamalandira zinthu ngati zimenezi matupi anu amakhala osangalala, potiphunzitsa malimidwe, Mmmm Pakatimpakati titi potiphunzitsa malimidwe. Chabwino. Aaaa, pakhalapo kusintha pa nkhani zokhudza udindo wa Abambo. Mayi, kapena anyamata ndi atsikana kumbali ya madyedwe chifukwa cha ntchito za Care? Udindo kapena kusintha Kwa anyamata? KusinthaKwa maudindo. Maudindoo? Eyaaa. Maudindo asinthidwa ndithu, chifukwa choti kaya ndi asungwana, ali kukhala pa udindo, kaya ndi mzimayi, ali kukhala pa udindo, mosasankha mbali kuti kaya ndi azibambo ndi amene akuyenela kukhala pa udindo koma mzimayi panopa ndilo amene akukhala patsogolo kumakhala Chairman, chimene chatipangitsa kuona kuti chasintha zimenezi zasinthidwa kudzela mÕbungwe la Care. Timakhala mwina azimayi sikisi, mwina azibambo folo Mmmm. Koma izi zachitika chifukwa chophunzitsidwa ndi Care, chokhudzana mmaudindo mzimenezi. Apapa mufotokoza za maudindo a mbali ya Utsogoleri eti? Oh ee mmaganiza kuti maudindo ake ndi amenewo. Chabwino. Panali funso lina limene limabwera lokhudzana ndi mbali imeneyo ndiye kuti mwandiyankhilatu. Oh chabwino. Mwina nkutheka kuti mufuna muonjezelepo pa zimene mmafotokozazi, chimene chasintha kumbali ya mautsogoleri? Mautsogoleri? Munakamba za utsogoleri eti? Eee ndinawakamba. Kuti asintha motani, azimayi akumatengapo gawo, atsikana akumatengapo gawo, china nchani chimene mungafotokoze kumbali imeneyiyi? Yautsogoleliyi? Mmm Mbali yautsogoleriyi, yasintha mmene ndikunenela ndiye kuti palibe kusiyana kagwiridwe ka ntchito. Mukamati palibe kusiyana kagwiridwe ka ntchito mutanthauza chani? Ndiye kuti nzimayi kaya nzibambo, ntchito imene ayenela kugwira nzimayi, ndiye kutinso bambo ayenela kugwira, imene ayenela kugwiranso bambo mzimayiso ayenela kugwira, kugwira ntchito mofanan. Chabwino. Moti inu mphika mukhonza kugwira nkuphika nsima? Eee, popanda choletsa. Moti mwana, mwana mukhonza kumudyetsa phala? Eee popanda choletsa.Nzimene zasintha chifukwa cha bungwe la Care. Moti mzimayi akhonza kuwaza nkhuni? Eee Chabwino. Titengeno kumbali ya maudindo ena okhudzana ndi kadyedwe kenikeni ka, chasinthapo ndi chani? Mudindo yokhudzana ndi kadyebwe kenikenika? Eee. Pmenepa chasintha chifukwa chonena kuti, zija ndakamba kale, palikumasukilana, mzimayi, mzibambo tidye moyenelela posaika magawo oti ichi nchoyenelela ine bamboo kapena ichi nchofunikila ine mayi, koma chinthucho, chidyewe, chidyebwe mofanana ngati banja. Amene amasokolotsa zakudya ndi ndani pakhomo? Pakhomo timasokolotsa zakudya pokhalilana pansi. Chabwino. Tigwirizane kuti tipeze chakudya, ama timasokolosa chakudya pokhalilana pansi, timakhalilana pansi. Chabwino. Kumbuyoku zinkakhala bwanji, mmakhalailananso pansi kapena zayambika chifukwa cha Care yi? Kumbuyoko, zimenezi sizinali nkuchitika kwenikweni, mwina kumatheka bamboo ndiye amatenga gawo kwambiri. Koma pakali pano sizili choncho. Pakali pano tisanakonze chofunikila kuti chichitike, timayamba kukhalilana pansi, nchimene chaonetsa kuti chasintha. Chabwino. Chifukwa chotsatira ndondomeko ya ntchito za ku Care. Kumbali ya ntchito zakumunda, kagwiridwe ka ntchito zakumunda zumakhala bwanji, amagwira kwambiri ndi ndani kapena zimakhala bwanji? Kagwiridwe ka ntchito zakumunda, Mmmh. Kagwiridwe ka ntchito za kumunda mumakhala kugwira ntchito mofanana komanso mopatsana mpata monga nzimayi ukhonza kumpatsa mpata kuti aah inu tsopano tiyeni tiweruke poonetsa kuti tichite zinthuzo mosapanikizidwa. Timagwira ntchito komanso timalemekeza azimayi kuti tisachite zinthu moti wina achite ngati wapanikizidwa, koma tiwapatse mpata anzathu popeza amakhala ndi ntchito zambiri zomwe zija tinena, athyola ndiwo kaya anena kuti tengankoni nkhuni,ndiye kuti ntchito zija zimatipepukila tikamatengezana.Moti ntchito yakumunda kugwira kwake ndugwira koma mololelana mosatenga nthawi yosakwanila kwenikweni. Kumbuyoku zinkakhala bwanji, zimakhala chimodzimodzi kapena apa zasintha? APA zasintha chifukwa chotikumbuyoku kumatheka kuti aah tengani makasuwa ine ndisoseza nkhuni, ndiye zimaonetsa ngati munthu uja ali kugwira ntchito yolemetsa. Talima mofanana, ndiye kuti ali kusenza ntolo wa nkhuni, tili kumpatsanso makasu, zimene zijazo zidasintha. Chabwino. Ine ndutenga khasu ngati bambo, iye uja akutenga kaya ntindiwo ngati mayi nkumapita kunyumba. Wina watenga Nji, wagwira, watengako chida wina watenga chida. Zaintha chifukwa cha zimene mumaphunzira ndi a Care? Ndi a Care. Zimene zi Zasintha chifukwa cha chophunzitsidwa ndi a Care. Pa ziganizo zimene mmachita zokhudzana ndi ulimi zimakhala bwanji? Mmapanga bwanji ziganizo za ulimi? Ziganizo za ulimi, timazipanga pokhalirana pansi, kaya tagulitsa mbewu yathu, timanena kuti kodi ndlama ndi iyi tapeza, titani? Aaah tiguleko feteleza, kapena tionjezele chakudya. Koma pali kukhalirana pansi ngati banja. Kuti chaka chino tilima mbewu zakuti, ziiganizo amapanga ndani? Ziganizo zimenezi timapanga anthu awiri mÕbanja, tilime ntedza, tilimekonso ka soya tisangokhala choncho, tilimeko timbatatesi, chimanga ndiye popeza chimakhala mu pologalamu nthawi yonse. Tilime chimanga tionjeze, ngati idali one Ekala tionjezepo one Ekala, koma tili pokhalirana pansi. Chabwino. Asadabwere a Care munkapanga choncho ziganizo, kapena zachita kusintha? Aaaa zimenezi zasintha chifukwa cha bungwe la Care, kale timangomachitapo, mwina wekha wangoganizila, ayi apa ponse tilima ujeni, tilima fodya pamene pano timafunsana kuti kodi titani. Aaah gawo ilii tilimepo fodya, gawo ili nsawa, gawo ili tilimepo nsawa kapena kachewere, pamene kumbuyoku timangonena kuti apa tilima fodya, koma posafunsana. Chabwino.Inuyo mmaganizo mwanu Project ya Care yi mwaiona bwanji? Mmaganizo mwanga ndaiona kuti Project ya Care ndiyothandiza. Tafotokozani. Kuthandiza chifukwa choti ili kutiphunzitsa zinthu zoti moyo wathu ukhale wathanzi.Moyo wathu uthandizidwe, kuthandizidwako ndiye kuti pali thanzi, chifukwa tikuchita zinthu zofunikila pa miyoyo yathu chimene bungwe la Care lofunika kwambiri chifukwa latizindikilitsa zinthu zambiri. Tatchulaponi zinthu zitatu zimene zakusangalatsani Project imeneyi kapena zimene mwaphunzirapo? Zinthu zitatu, Timadimba tija tanena, komanso ngakhale ulimi wa kuntundawu Care yatiphunzitsa,tikhonza kutchulanso ngakhale mitengo ya zipatso ngakhale yoti si yazipatso. Mwaphunzira ku Care kokhakokhako? Care yatiphunzitsa zimenezo kuti tikhale anthu osatani kodi, odzidalira. Chabwino. Pakukhala kwathu. Ndi ziti zimene simunazikonde mu Project imeneyi ya Care? Mu Project ya Care sindinganene kuti, sindidaa, ichi sindidachikonde chifukwa zimene tuphunzitsidwa nzonena kuti anthu akuzilandira komanso zuthandiza munthu pa moyo wake. Chabwino. Inuyo ngati a Group a Mfumu Msangwa mukuona kuti Project ya Care yi yabweretsadi kusintha mmudzi muno? Eeee Ngati Pali kusintha tafotokozani kusintha kwake nkotani? Kusintha kwake mmadyebwe abwino, komanso anthuwo akakhudzidwa ndi chinthu choti auzidwe amamva mwa changu, zimenezi zasintha chifukwa cha Care. Pali ukhondo, ndipo titakhala kuti tiyende kuyendayenda aah pamakhala zinthunso zosintha, ngakhale midzi Ina imadzionela kuti mmudzi umu muli upangili, koma upangiliwo tsono, uli kubwera chifukwa cha bungwe la CARE. Chabwino.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_404.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_405.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_406.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_407.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_408.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_409.wav
180
210
./data/chichewa-dataset\audio\segment_410.wav
210
240
./data/chichewa-dataset\audio\segment_411.wav
240
270
./data/chichewa-dataset\audio\segment_412.wav
270
300
./data/chichewa-dataset\audio\segment_413.wav
300
330
./data/chichewa-dataset\audio\segment_414.wav
330
360
./data/chichewa-dataset\audio\segment_415.wav
360
390
./data/chichewa-dataset\audio\segment_416.wav
390
420
./data/chichewa-dataset\audio\segment_417.wav
420
450
./data/chichewa-dataset\audio\segment_418.wav
450
480
./data/chichewa-dataset\audio\segment_419.wav
480
510
./data/chichewa-dataset\audio\segment_420.wav
510
540
./data/chichewa-dataset\audio\segment_421.wav
540
570
./data/chichewa-dataset\audio\segment_422.wav
570
600
./data/chichewa-dataset\audio\segment_423.wav
600
630
./data/chichewa-dataset\audio\segment_424.wav
630
660
./data/chichewa-dataset\audio\segment_425.wav
660
690
./data/chichewa-dataset\audio\segment_426.wav
690
720
./data/chichewa-dataset\audio\segment_427.wav
720
750
./data/chichewa-dataset\audio\segment_428.wav
750
780
./data/chichewa-dataset\audio\segment_429.wav
780
810
./data/chichewa-dataset\audio\segment_430.wav
810
840
./data/chichewa-dataset\audio\segment_431.wav
840
870
./data/chichewa-dataset\audio\segment_432.wav
870
900
./data/chichewa-dataset\audio\segment_433.wav
900
930
./data/chichewa-dataset\audio\segment_434.wav
930
960
./data/chichewa-dataset\audio\segment_435.wav
960
990
./data/chichewa-dataset\audio\segment_436.wav
990
1,020
./data/chichewa-dataset\audio\segment_437.wav
1,020
1,050
./data/chichewa-dataset\audio\segment_438.wav
1,050
1,080
./data/chichewa-dataset\audio\segment_439.wav
1,080
1,110
./data/chichewa-dataset\audio\segment_440.wav
1,110
1,140
./data/chichewa-dataset\audio\segment_441.wav
1,140
1,170
./data/chichewa-dataset\audio\segment_442.wav
1,170
1,200
./data/chichewa-dataset\audio\segment_443.wav
1,200
1,230
./data/chichewa-dataset\audio\segment_444.wav
1,230
1,260
./data/chichewa-dataset\audio\segment_445.wav
1,260
1,290
./data/chichewa-dataset\audio\segment_446.wav
1,290
1,320
./data/chichewa-dataset\audio\segment_447.wav
1,320
1,350
./data/chichewa-dataset\audio\segment_448.wav
1,350
1,380
./data/chichewa-dataset\audio\segment_449.wav
1,380
1,410
./data/chichewa-dataset\audio\segment_450.wav
1,410
1,440
./data/chichewa-dataset\audio\segment_451.wav
1,440
1,470
./data/chichewa-dataset\audio\segment_452.wav
1,470
1,500
./data/chichewa-dataset\audio\segment_453.wav
1,500
1,530
./data/chichewa-dataset\audio\segment_454.wav
1,530
1,560
./data/chichewa-dataset\audio\segment_455.wav
1,560
1,590
./data/chichewa-dataset\audio\segment_456.wav
1,590
1,620
./data/chichewa-dataset\audio\segment_457.wav
1,620
1,650
./data/chichewa-dataset\audio\segment_458.wav
1,650
1,680
./data/chichewa-dataset\audio\segment_459.wav
1,680
1,710
./data/chichewa-dataset\audio\segment_460.wav
1,710
1,740
./data/chichewa-dataset\audio\segment_461.wav
1,740
1,770
./data/chichewa-dataset\audio\segment_462.wav
1,770
1,800
./data/chichewa-dataset\audio\segment_463.wav
1,800
1,830
./data/chichewa-dataset\audio\segment_464.wav
1,830
1,849.676938
./data/chichewa-dataset\audio\segment_465.wav
Aaah tili kuno Kwa a Nsangu, Nsangwe? Msangwa. Msangwe? Tili ndi a Community leader, Alifeyo, Sandram. Alifeyo Sandram. Chabwino. Aaa Funso lathu loyambilira, timafuna tidziwe nawo kuti kodi udindo wanu mmudzi muno ndiwotani? Ok, ineyo ngati Lifeyo Sandram udindo wanga ndiwoti ndine Promoter amene ndimaphunzitsa za Kadyedwe koyenela kuchokera ku bungwe la San Project. Ohoo. Yaah. Ndithu Chabwino. Mwakhala mukutengako mbali, Mwakhala mukutenga mbali yotani pa zintchito za chitukuko za Sani. Aaa ineyo ngati Promoter, ndakhala ndikutengapo gawo ku nkhani zosiyanasiyana , one aah ndimaphunzitsa anthu za kadyedwe koyenela, two aah ndimaphunzitsanso kuti adzikhala mmagulu a kusunga ndi kubwereketsa kuti kumene kuja mwina akamatha kusungako ka ndlama kaja adzikhala ndi gawo loti nthawi ina ngati ka ndlama kavuta pakhomo paja ndiye kuti adzipeza gawo loti ka ndlama kamene kaja adzikakatenga ku gulu la kusunga ndi kubwereketsa lija kuti adzitha kugula ti zakudya tina mwina ta magulu six kuti pakhomopo lisamavute. Ohoo Komanso kuchokera apo takhala tikuphunzitsa nkhani za ukhondo kuti ngati munthu akudya zakudya zamagulu asanu ndi limodzi, six! Ndiye kuti munthu ameneyu banja lake layenekela kukhala la thanzi ndithu.Takhalanso tikuphunzitsaponso zinthu zosiyasiyana monga kakonzedwe ka zakudya za magulu asanu ndi limodzi six, kuti mwina timatha kupita mwina mudzi ndi mudzi ndithu kumawaphunzitsa kuti atha kupanga zakudya za magulu asanu ndi limodzi six, ndiye timathanso kuwafotokozelanso kuti mwina kupez akumatha kukhala kovuta koma munthu wayenekela adzidya zakudyamwina patsiku zosachepela za magulu anayi. Ifeyo ngati ma Promoter timaphunzitsa zimenezo, ndiye timalumikizananso ndi anzathu ngati ma lead farmer mu Project yomweyi ya Sani, amene aah timatha kuthandizananso kuti aa, aliyense amene mu Care group, wayenela adzilima mbewu zosiyasiyana ndi cholinga chakuti zokudya za magulu six amene zimene timawaphunzitsazo zisamakhale zovuta, moti timawaunikila kuti adzikhala ndi madimba a pakhomo. Mmm Ehee, Ngati mu nkhani za Ukhondo, ndiye timawalimbikitsa kuti adzikhala ndi chimbudzi chimene chikugwira bwino ntchito. Ohoo. For instance mwina ngati munthu pakhomo alibe chimbuzi chogwira bwino ntchito ngakhale atamadya zakudya za magulu asanu ndi limodzi six, ndiye kuti Ukhondo pakhomopo udzikhala ovuta ndiye kuti matenda adzikhala nafalikila. Ohoo. Ndithundithu. Chabwino, chabwino. Ayi apopo mwakambapo ndithu zinthu zita, zochulukilapo ndithu, tayamikila. Aaah, Mwakambapo kuti mmagwiranso ntchito limodzi ndi ma lead farmer kuti anthu adzikhala akumalima mbewu zosiyasiyana, ndi mbewu zanji zimene inuyo mmaonetsetsa kuti anthu amenewa akulima? Mmm mbewu zimene mwina timatha kumalumikizana ndi ma lead farmer kuwalimbikitsa anthu osiyanasiyana a ma Care group kuti azilima, aaa mbewu zoyamba ndi za mÕgulu la zamasamba, timagwiritsa zimenezo kuti ngati ali ndi kadimba adzilima ndiwo zamasamba monga zimene zimakhala ndi ntundu wa green, cholinga chake ndichakuti mbewu zimenezi akamadya pakhomo paja adzikhala kuti akudya mbewu za mÕgulu la masamba komanso kuchokera apo timawalimbikitsa kulima chimanga chimene chimakhala cha ntundu wa Yellow. Ohoo. Mmene chimanga chija akachi akamadya, kaya akakagaya ufa uja ndiye kuti mmapezeka Vitamin A, ndiye kuti zimene zija zingakapangitsenso kuti mwina chifukwa cha ka nchere kameneko kamene kamatchedwa Vitamin A, ana aja akamalandira ana a Under 5, kaya azimayi oyembekezela, kaya azimayi oyamwitsa ndiye kuti zimatha kumapindula mmatupi awo kuti azipeza Vitamin A. Kuchokera apo ngati a Sani Project anatipatsanso mbewu through Care, mbewu ya Chinangwa.Mbewu imeneyi anatipatsa ndithu imenenso tina, timalima tili ndi minda yachitsanzo ehe kumene timaalimbikitsa kuti adzidzala mbewu ya chinangwa komanso anatipatsanso mbewu ya mbatata ya kholowa imenenso timailima. Aaah Mbatata yake sikuti aah sikuti ndi mbatata wamba, imene inalinso ya chikasu nkati, imenenso akamadyanso mbatata ija amakhala ndi mwayi oti amapezako Vitamin A Chabwino, chabwino. Eya. Aaah tsopano timafuna tioneno za miyambo ndi zikhalidwe kuti kodi anthu a mÕdela lino amakhulupilira, amakhulupilira zotani zokhudzana ndi za madyedwe komanso ndi udindo wa amayi ndi abambo? Ok aaah ngati anthu a mÕdela linolo, kumbuyoku, ndikamba za kumbuyo pangÕono mundikhululukila. Aaa kumbuyoko kumakhala miyambo ndi zikhulupiliro zosiyana siyana mwina chikhalidwe aa ngati kumbuyoku bungwe la Sani lisanabwere through Care Malawi ndiye timmapezeka kuti anthu amakhulupilira kuti ngati nzimayi oyembekezela ali oyembekezela ndiye kuti amalola kuti asadye nthochi zomatana. Oh nthochi zomatana ayi? Eeeh Nthochi zomatana asadye, chifukwa choti akadya nthochi zimenezo aah akuti panali zikhulupiliro zoti akhonza kudzaona ana wiri ameme amatchedwa ma twins ma pasa, Oho, okey Eee ndiye aaa pakafukufuku wathu ngati ifenso a Care ngati ma Promoter, ma lead farmer VA titakhala pansi tinakaona kuti zimenezo ndi za bodza aa ndiye zimangopangitsa kuti ngati mzimayi sadzidya nthochi chifukwa choti mayiyo ndioyembekezela ndiye kuti gulu la zipatso nthupi mwake lizikhala loti likuvuta,ndiye timayesetsabe kuwalimbikitsa kuti sibwino kuti adzikhulupilira zinthu ngati zimenezo, ndikwabwino kuti adzidya nthochi ndithu ngati mayi oyembekezela ndi cholinga choti aah zakudya zamaguluzo mnthupi zisamachepe. Aaah panalinso chikhulupiliro china choti mwina aa mwana amene ali under 5 asadye maungu, Ohoo Eee timati maungu, ndiye amati mwana akamadya maungu amene ali Under 5 aah mwina amadzadwala matenda ena amene amawatcha mauka.Ndiyebe pokhala pansi timawaphunzitsa kuti zimenezi ndi za bodza ndithu mwana ngati wakwanitsa miyezi six, chifukwa mmaungumu muli timichere timene timapezeka mÕgulu la zamasamba ndiye timichere timeneto tikhonza kumuthandizila mwanayi asanyentchele kapena asapinimbile. Chabwino, chabwino. Ndiye pakali pano zikhulupiliro zimenezi zinakachitikabe? Aaah ngati kuno kwathu zikhulupiliro zimenezi ndi misonkhano imene timakhala nayo yowaphunzitsa aa nkhani zimene a Sani Project anabwera nazo zatha, sitingati zachepa koma zatheratu chifukwa choti aliyense panopa ali nkuthekera koti tikamawayendela tikuona ndithu kuti anawa akumatha kumadya zinthu zosiyasiyana zimene zimapezeka ndi michere yosiyasiyana imene imawathandiza mmatupi mwawo. Chabwino. Ndithu, ndithu. NangaÉ Chabwino ayi apopo mwatambasulapo ndithu nkhani zinthu zambiri ndithu. Nanga pamaudindo Wa amayi ndi abambo pankhani ya za madyedwe wasintha motani? Chabwino. Aaa Mwina tingobwerezanso yaa kuti tinene kutiÉnanga, Ok Chabwino. Apo talankhulapo ndithu mwatifotokozelapo ndithu mwaaa, mwamvemvemve zokhudzana ndi kadyedwe komanso ndi zikhulupiliro, Nanga udindo wa amayi ndi abambo wasintha motani,kapena kuti mmbuyomu unali otani ndipo panopa wasintha motani? Ok pankhani ya udindo wa amayi ndi abambo panopo wasintha, kumbuyoku ngati dela lathu lino zinali zomvetsa chisoni kwambiri, ndikamanena zimenezi mundimvetsetse ndithu kuti ngati zaka zapita kumbuyoku ngati Sani isanabwere through Care Malawi ndiye kuti kumapezeka kuti azimayi amagwira ntchito mwina zobzola nsinkhu wawo mwina ife azibambo timangotengela kuti ntchito zambiri zapakhomo oyenela kugwira ndi mayi, komabe chifukwa cha Pologalamu imene anzathu a Sani anabweretsa through Care Malawi yoti tidzikambirana nawo za Gender mma Care Group mu zimenezi zatithandizila kwambiri kuti panopa azibambo akumatha kumvetsa kuti mzimayi wayenela kugwira ntchito maganizilidwa. Tikamati kuganizilidwa ndiye kuti tikutanthauza kuti pamene akugwira ntchito pakhomo pa tsiku ndiye kuti aziona kuti kodi mzimayi akhonza kugwira ntchito zochuluka motani, nanga mzibambo akhonza kugwira ntchito zochuluka motani. Ndiye chimene tikutanthauza pamenepa nchakuti, ntchito zimene mwina ngati kumbuyoku azibambo amaona kuti nza nzimayi yekhayekha panopa azibambo ali nkuthekela koti akumathanso kugwira ntchito zimenezo, mwina kapangidwenso ka ziganizo pakhomo pamakhala gawo lina loti mwina pakhomo paja pakufunika papangidwe ziganizo kapena mfundo, ndiye kuti mabanjawo panopa akumatha ndithu kupangila limodzi ziganizo za pakhomo kapena kumapatsana mpata mmene ndanenela pa kagwiridwe ntchito ka pakhomo pa tsiku ndithu. Chabwino. Ndithu, ndithu. Ayi apopo tiyamika kuti mwatambasulako kochuluka ndithu zokhudzana ndi kagwiridwe ntchito ka amayi ndi abambo, palinso china chilichonse chimene chilipo chimene mukhonza kuonjezela pa zimene anthu akuchita pa,pa udindo wa amayi ndi abambo pakali pano? Mmm, Eee chilipo ndithu aaa, ngatinso mwina pakati apa mwayi ndi mphamvu timadziwa kuti pakhomo pamakhala katundu osiyasiyana, ngati zaka zapita ku mbuyomu Sani isanabwere, zimatheka kuti mwina pakhomo paja ngati pali katundu mwayi ndi mpjhamvu umakhala ku mbali imodzi. Abambo ndi amene amakhala ndi mwayi ndi mphamvu pa akatundu pakhomo ndiye as a result kumapezeka kuti mayi uja samakhala nkuthekela koti mwina akhale ndi mwayi kapena mphamvu pa katundu amene ali pakhomo, koma titawaphunzitsa, ee timakamba pa nkhani ya mwayi ndi mphamvu, panopa tikusiyanitsa ndithu kuti titawaphunzitsa kuti azimayinso ali ndi mwayi ndi mphamvu pa katundu amene ali pakhomo, zasintha ndithu kuti azimayinsoa akumatha kukhala ndi kuthekera kolamulira pakatundu amene ali pakhomo. Aaa pakasungidwe ka ma Committee a mmudzi, chimenechinso ndi chinthu chimene chasintha kwambiri kuno kwathu chifukwa cha ntchito za Sani Project. Aaa Sani Project itabwera kumbuyoku maudindo ambiri amatenga ndi azibambo okha okha. Kaya mwina tingoyerekeza kuti pali VDC mu dela mwina zimapezeka kuti azibambo ambiri ndi amene amakhala mma Committee amene aja, koma panopa chifukwa cha Upangili ndi Uphungu umene umachokela ku Bungwe la Sani Project, zatisinthila ndithu for instance mmudzi tili muno mwa Msangwa ndiye kuti Chair wa VDC ndi mzimayi. Ohoo Which means chifukwa cha upangili umene wachokera ku bungwe la Sani zatipindulira ndithu kuti azimayi akumathanso nkukhalanso nkuthekela komatha kutsogolera ma bungwe akuluakulu, komanso aa titagwirizana kumene timagwira ntchito ngati kunoko ndiye kuti nkwa GVH Nkanakufa amene, GVH imeneyo yakalumikizana ndi kwa TA, kwa Gogo Chalo, kwa TA Kayembe ndiye titaperekanso upangili wathu ndi uphungu umene timaphunzitsa mmamidzimu ndiye kuti chatikomelanso kuti masankhidwe a amayi mma udindo osiyanasiyana ngati akumudzi ndiye kuti ADC Chair ndiye kuti wapezekanso kuti ndi nzimayi.Ndiye kuti titaafunsa titaapanga interview ananena kuti zonsezi zabwera ndi kuthekera chifukwa cha uphungu umene timaphunzitsa wa za Gender wochokera ku Sani Project.. Chabwino. Ndiye kuti kusonyeza kuti Sani Project kuno kwathu yaah tisaname pa nkhani ya Gender yatipindulira kwambiri amene ali ma udindo osiyanasiyana. Chabwino. Ndithundithu. Ndiye titati tiike mma percentage kuti aah kutengako nawo gawo kwa azimayi, aaa tingakuike kuti ndi ma percentage angati mu zinthu za Gender izi? Mmm Panopa if we compare ndi kumbuyoku ndi panopa, ndiye kuti ma percentage amene tindingaike ineyo ndithu tatengela kuika pa 80 percent. 80 percent. Ndithu, ndithu. Chabwino, oho, chabwino. Aaa mwakhudzapo ndithu pa nkhani yoti pa zaka zitatu zimene Care yakhala ikugwira ntchito mÕdela linolo pakhala kusintha, mwina nkutheka kuti pa nkhani ya Gender imeneyii, chabwino aaa ndiye ndimangofuna kuti, ndimafotokozela kuti ndimafuna mwina mungotipatsa chithunzithunzi kuti aaa ndi azimayi angati kapena ndi ma percentage angati a azimayi amene akutengapo mbali mu ma, mu zinthu za Gender izi ngati kukhala mmaudindo otsogolera ndi amene asakutenga mbali, kuti tufuna tikhale ndi chithunzithunzi cha mbali zonse ziwiri. Ok. Eee kuti kukulemelela ndikuti, kumene kukutenga mbali ku, kumene kukutenga nawo mbali mu zinthu za gender izi kapena iyayi. Ok Ndithu ndithu. Mmm Pamene pa ndingayankhe moti ma percentage ngati mmene mwafotokozelamo, mwandifunsilamo, Mmmh. Aaa kumene kukutenga mbali ndi kumene Si kukutenga mbali kwambiri, ndiye kuti zikutanthauza kuti panopa ndiye kuti nkumene kukutenga mbali kwambiri ndikumene kukuchulukilako ndiye kuti titha kuika pa 60 percent kwa amene akutenga nawo mbali, 40 percent kwa amene sakutenga nawo mbali Chabwino. Ndithu ndithu, ndi mmene zasinthila. Chabwino, chabwino. Ndiye mukuona kuti ku 40 percent chapangitsa kuti mwina tisafikile konse kuti 40 percent ibwere nawonso uku kwinaku ndi chani kwenikweni? Mmmm, pamenepa ndiye kuti tingayankhe kuti zimakhala zovuta kuti mwina uthenga uja uwafikile onse mofulumila pa nthawi yake eehe chifukwa choti pali ena amazizi kwambiri makamaka azimayiwa mwina ukakhoma nsonkhano, mwina ukaitanitsa nsonkhano satha kubwera onse ndithu, ndiye kagulu kamene kamalephera kukafika ku nsonkhano kaja ndikamene tikukaika ngati ku 40 percent ku. Chabwino. Koma akanakhala kuti anthu amenewa nthawi imeneyo ankapanga participate amabwera ndiye kuti tikanati 100 kumene koma chifukwa choti anthu ena amalephera kukalumikizana nafe ngati ku mikumano tikunenayi. Eeee Ndiye nchifukwa chake tanena kuti 40 percent imeneyi ndi imene yachita ngati ikutsalira. Nanga kwa abambo potenga nawo mbali ku zintchito za gender izi ma percentage ake mungawaike bwanji? Mmm abambo tingawaike 70 percent. 70? 70 percent. Ohoo. Ndithu ndithu. Chabwino, chabwino. Which means 30 percent ndi imene ikuchitika ngati ikutsalira. Chabwino. Ndiye kuti 30 percent vuto lake linali ngati lomweli la kwa azimayili kapena kunali vuto linanso? Mmm ngati azibambo, ndiye kuti vuto lake ndilosasiyananso ndi la kwa azimayili. Ohoo. Eee. Chabwino. Ndithu, ndithu. Aaah chabwino, tsopano panopa tufunano tioneno za kafukufuku wa mmudzi , aah aah ndimafuna mundiuzeko za zochitika, za zochitikachitika zimene zili zazikuluzikulu zimene zinachitika kuchokera mu 2018 pamene Project imayamba kudzafikila pamene Project yi imalekelapa eti? Ehee. Kuti ndi zochitika ziti zimene zachitika zimene zisali zokhudzana ndi Care komano zaa ndinganene kuti zakhudzana ndi nkhani ya madyedwe,eti? apapa tikutanthauza kuti kukhonza kukhala kuti kunachitika, mwina kunagwa mbozi zimene zinasokoneza chakudya, mwina zitha kukhala kuti kunabwera bungwe lina lake klinadzagawa chakudya zimene zathandizilanso pa za madyedwe, kapena mwina kunabwera ena ake koma sanali ochokera ku Care koma anazaphunzitsa zokhudzana ndi za madyedwe, kapena mwina anadzagawa kaya mwina ndi Chiponde kwa ana, Mmmh. Ehe, kaya mwina kunali kusefukila kwa madzi kapena mwina kunachitika chinachake chimene ndithu chinali chachikulu koma chachitika aaa mu zaka zitatu zimene Care inali kugwira ntchito? Ok. Ndithu. Mmmh pa zaka zitatu zimenezi ndiye aah tisaname zinthu zimene zinabwera zinatipinga ndithu ngati kulowa mchaka chinochi, chakudya chimene tatuluka nacho chinali chovuta kwambiri kufika chaka chino? Eeeh kufika chaka chinochi, tatuluka nachochi chinali chovuta kwambiri. Ndiye kuti tikuyambila 2019, mpakanaÉ 2020? Mpaka 2020, Ehee chifukwa choti 2019 yi tinakumana ndi zinthu zingapo, One tinali ndi mbozi zimene mukunenazo zinkadya kunsonga ndithu kwa mmera wa chimanga, as a result chimanga chija sichinachite bwino. Ndiye kunabweranso aaah mmh Mphuzi zimene zinkadya kumizu ya chimanga, ndiye as a result chimanga chija ndiye kuti sichinakule chinapinimbila ndithu, kunapezeka kuti anthu sanakolole, thatÕs why ndiye kuti chakudya chinadula kwambiri chifukwa makomo ambiri analibe chakudya, moti ndi chimene chinatipsinja kwambiri. Aaah ndiye kuti tidziti zangochitika za tsundanatsundana mzaka zonse zimene a Care amagwira ntchito kuno through Sani Project, ndiye kuti ti mbozi timeneti takhala tikuononga kwambiri zaka zimenezi. From 2017 mpaka panopa moti ngakhale mmindamo tikuoneka ndithu zimene zikupangitsa kuti mbewu yathu ya chimanga sinachite bwino kwambiri so as a result tilibe ndi nkhawa kuti aah gawola njalali ndiye kuti lipitililabe zimene zitipatse nkhawa kuti kukhudzana ndi ana a Under 5 azimayi oyembekezela kuti ali pavuto lalikulu kwambiri kuti ngati mzimayi ali oyembekezela ngati zakudya mokwanila ndiye kuti akhoza kunyentchela. Chabwino. Ndithu, ndithu. Chabwino. Ndiye zi mavuto amenewa, chabwino aah paja mmafotokoza kuti, mwafotokozapo kuti zabweretsa mavuto amadyebw, ndimafuna ndingodziwa kuti palinso mavuto amene adza Kamba ka mavuto amenewa? Mmm mavuto ena tingati ndiye kuti its financial problems . Ohoo. Eee chifukwa choti mwina aah chimanga sichikuchita bwino chifukwa cha Mbozi zimenezi ndiye kupezeka kuti ngakhale kapezekedwe ka ndalama pakhomo kakumakhala kovuta kwambiri. Ohoo. Chifukwa ndiye kuti tikumangodalira mbewu imodzimodzi kuti iti itipatse ndalama, so as aresult ndiye kuti kukumakhala kovuta kuti throughout the year, mukhale kuti muli ndi ndalama yokwanila pakhomo, ndiye kuti zimenezi zikutipatsanso nkhawa kuti ngati mmene anzathu a Sani Project through Care Malawi eee timapelekapo Upangili kapena maphunziro athu ndiye kuti mwina gawo limodzi kukhoza kukhala kovuta kwambiri kuti zintchito zikhazikike ngati mmene timazionela zinakhazikikila. Chabwino. Ndithu, ndithu. Chabwino aah, sikunabwereko mabungwe ena kudzapanga zokhudzana ndi za madyedwe? Ayi kunoko sikunabwereko mabungwe ena alionse. Sanafike? Chabwino. Ndithu ndithu. Aaah chimene chinapangika ndi chakuti mmh Pali midzi ina imene ili Under TA Kayembe ndiye kuti ili ndi Vision, World Vision. Ohoo. Eeeh, pamene tikatenga ngati Msangwa ndiye kuti kulibe World Vision. Chabwino. Eee ndiye midzi ina imene ineyo ndinkaphunzitsako za madyedwe oyenela ndiye kuti ili under World Vision pamene midzi ina sili under World Vision.Ndiye ngati for instance Msangwa village ndiye kuti sali mu World Vision pamene Ndendela imene ma members ena munacheza nawo ali mu World Vision. Ohoo. Ndiye ngati ku Ndendela ku ndiye kuti bungwe la World Vision nalonso likumaphunzitsa nkhani za madyedwe. Ohoo, cahbwino. Ndithu koma ngati Msangwa uno ayi sikunabwereko bungwe lililonse lophunzitsa za madyedwe. Sikunagawidwekonso zakudya? Ayi Sikunagawidweko chakudya chilichonse. Chabwino. Ndithu ndithu. Chabwino. Tsopano chasintha kwambiri mmudzi muno pa nkhani ya madyedwe oyenela ndi chani? Ok chimene chasintha kwambiri mmudzi unowo ku nkhani ya madyedwe oyenela ndi ngati Uphungu umene anthu amalandira. Ohoo. Chifukwa ndikukhulupilira kuti amanena kuti, pa Chichewa amanena kuti munthu ndi bwino umupatse mbeza yoti iye uja adzitha kukaweza Nsomba kusiyana kuti udzimpatsa Nsomba kuti iye uja azidya, kusonyeza kuti munthu akangodalira kuti ndidzingodalira zomwe walandira. Ohoo. Kusonyeza kuti munthu akumadalira kuti ndidzingolandira kumakhala kovuta kwambiri kusiyana kuti munthu uja alandire uphungu. Ndiye chifukwa cha uphungu umene anthu alandira kuchokera ku Sani Project aah, Uphungu umenewu awugwilitsitsa kwambiri, motitu panopa anzathu tinayamba nawo ndiye anthu akudya za magulu sikisi. Ohoo. Zimene kumbuyoku sizikmachitika, ndiye kuti zasintha kwambiri, kuti akumatha kudziwa ndithu kuti ayi mwina ukadya ndiwo za nkhwani ndiye kuti wadya za mÕgulu la masamba, mwina ukadya nyama wadya za mÕgulu la nyama, mwina ukadya nyemba ndiye kuti wadya gulu la nyemba, mwina ukadya Mango ndiye kuti wadya gulu la za Mango, ndithu kuti anthu akutha kumikisa ndithu kuti akumatha kudya zakudya za amagulu onse, mwina ngati achepekeledwa akumayesetsa ndithu kudya zakudya za magulu anayi. Chabwino. Ehee zimene zo nzimene zatisinthiala kuti uphungu wakhazikika ndithu. Chabwino. Ndiye mwati uphungu umenewu wadza Kamba ka Sani Project. Ohoo. Chabwino. Ndithu, ndithu. Chabwino. Aaa pali kusintha kulikonse pa nkhani yokhudzana ndi za madyedwe oyenela, aah makamaka pa udindo wa amayi, abambo, anyamata ndi atsikana monga popanga ziganizo zokhudzana ndi madyedwe? Limenelo mundibwerezelako. Chabwino. Aaah. Pamenepo Pali kusintha kwakukulu ndithu kumene kwaoneka, mmh tikatengela ngati ku magawo a zamagulu mmene ndikunenelamo a magulu a zakudyawa kumatheka kuti kumbuyoku tikapha nkhuku pakhomo, nkhuku ija mwina kumapezeka kuti pakhomo paja timakhala ndi chikhulupiliro choti aa Nkhukuyi, Teteya, tili ndi gawo lina la Nyama limene timalitcha Teteya. Ohoo. Gawo limeneli ndithu amayenela azidya ndi abambo mayi asatani, asadye. Asadye. Mwina Ntchafu adzidyanso ndi abambo, ndiye zimenezi chifukwa cha Upangili umene ndakhala, tikuphunzitsa, ndiye kuti zasintha kuti aah sibwino kuti abambo adzipatsidwa gawo lalikulu la chakudya pamene mwina amayi akudya gawo lochepa iyayi kuti mayi uja akumakhala ndi kuthekela kodya Teteya mwina Ntchafu. Ohoo. Ehee, ndiye ngakhale mwina kukhudzananso ndi atsikana mwina amatha kumatha kumadya pangono chakudya, mwina za magulu osiyanasiyanawa chifukwa choti gawo lalikulu limapita kwa abambo,kumbuyoku kumenekoko, koma ngati panopandithu pakumatha kukhala kuthekera koti magulu onsewa atsikana, anyamata, abambo, amayi, akumadya ndithu mofanana. Ohoo. Ehee. Chabwino. Ndiye mwakambapo za Teteya, Teteya akutanthauza kuti chani? Mmm Teteya, Hee aah chimenechi ndii ngati gawo limodzi la nyama ya Nkhuku ee, chimapezeka kumbuyo kwenikweni Kwa Nyama ya Nkhuku. Ehee Ena Amati Chinyomphilo? Eee Chinyomphilo Ohoo. Chifukwa cha mmene chimakomela bamboo amangoonetsa kuti iyeyu, mmene amakomela chinyophilochi, ndiye kuti mayinso adzidyako ayi, Ehee Koma mmene amachimvela bamboyo, ndiye kuti chidzingokhalakwa bamboo. Chabwino. Aah panopa tikufuna tikambirane zokhudzana ndi kusintha aah kwa Project imeneyi. Inuyo mmaganizo mwanu, Project imeneyi mukuiona bwanji, ya Sani? Mmm ineyo pakutengela kusintha Kwa Project imeneyi, ndikuyiona kuti, anatipatsa kuti Project yi its ya zaka five. Ohoo. Koma pa zaka five, zaka zimene yaonekelapo kuno ku field ndi zaka zitatu. Ohoo. Ndiye kuti as a result ngakhale tikunena kuti zinazo zasintha komabe Project yi aaa pazimene inatibweletselazi ikanakhala kwa zaka five, ndikukhulupilira kuti kudakanakhala kusintha kwambiri, motero timafuna kupemphako kuti ngati pangakhale kuthekera mwina a Care wo atatibweletselanso mabungwe ena okhudzana ndi nkhani ngati zomwezi,kaya ngatikungapezeke mabungwe ena ndithu ophunzitsa za madyedwezi, atabweranso ndithu kuti zizachite ngati zakhazikika, zaka five zo, inde zinali zambiri koma potengeela ndimmene anatifotokozelera kuti Sani ikhala kuno tinadzitenga ngati zochepa. Chabwino. Ndiye ndikwabwino kuti mwina mabungwe ena atapezekanso ophunzitsa za madyedwe oyenela, atatibweretsela kuti adzachitenso ngati awonjezela pamenepo, chifukwa amati Mphini yobweleza bweleza ndiimene imatupa. Ohoo Eee Chabwino. Aaa Tsopano apopo mwangolambulira cha mmwambamwamba, aah Project imeneyiyi inuyo mukhonza kufotokoza kuti mwaikonda, kapena inuyomwakondapo chani pa Project imeneyiyi, ndipo ndi ziti zimene inu simunakondepo pa Project imeneyiyi? Mmm mu Project imeneyiyi ndiye kuti ine ndiziti zimene ineyo ndazikonda ndiye nzochuluka, Ohoo One kuno kwathu nkhani ya za mabungwe zi ndiye ndikumbali Mmmh. Ndiye kuti itabwera Sani Project through Care Malawi kuno kwathu ndiye kuti yatisangalatsa kwambiri, kuti nkhani za Gender muja ndanenela kuti zinali za kumbali timangozimvera mmbalimo, koma kunoko anthu atalandira upangili, anthu atalandira uphungu ndiye kuti kwapezeka kuti anthu ambiri akutsatira. Nkhani za madyedwe oyenela mm mwina timangodzimveranso mmbalimo, koma chifukwa cha Sani Project itabweretsa ma Program awo, powaona kuona ndithu kuti mmh kani mzimayi oyembekezela amyenela adzidya za magulu za amagulu asanu ndi imodzi six, zimenezi kwa ine zandisangalatsa kwambiri, nzimene zandipatsanso chidwi kwambiri moti bungwe limeneli latithandiza kwambiri, moti chifukwa cha chimenechi aah zatithandiza Nkhani Ina ndi nkhani ya za ukhondo eeh, kuti ngati munthu ali wa ukhondo, ndiye kuti munthuyi matenda amakhala mÕdani kwa iye. Kutanthauza kuti munthu ngati pakhomo ali ndi chimbudzi choti chikugwira, amasamba mmanja, Pali chovindikila pa dzenje, aa mwina kaya soap akupezeka kumeneko kuti akadzithandiza akatuluka asambe mmanja ndiye kuti adzikhala a ukhondo adzikhala otetezedwa ku matenda. Zinthu ngati zimenezi ndizoti zatithandiza kwambiri kuti kuno dela lathu zasintha. Ohoo. Moti Care Malawi tikuithokoza kwambiri ndithu pa zimene inabweretsa kuno kuti chifukwa cha chimenechocho zatipangitsa kuti zambiri dela lathu lino zizinthe. Chabwino.
0
30
./data/chichewa-dataset\audio\segment_466.wav
30
60
./data/chichewa-dataset\audio\segment_467.wav
60
90
./data/chichewa-dataset\audio\segment_468.wav
90
120
./data/chichewa-dataset\audio\segment_469.wav
120
150
./data/chichewa-dataset\audio\segment_470.wav
150
180
./data/chichewa-dataset\audio\segment_471.wav
180
210
./data/chichewa-dataset\audio\segment_472.wav
210
240
./data/chichewa-dataset\audio\segment_473.wav
240
270
./data/chichewa-dataset\audio\segment_474.wav
270
300
./data/chichewa-dataset\audio\segment_475.wav
300
330
./data/chichewa-dataset\audio\segment_476.wav
330
360
./data/chichewa-dataset\audio\segment_477.wav
360
390
./data/chichewa-dataset\audio\segment_478.wav
390
420
./data/chichewa-dataset\audio\segment_479.wav
420
450
./data/chichewa-dataset\audio\segment_480.wav
450
480
./data/chichewa-dataset\audio\segment_481.wav
480
510
./data/chichewa-dataset\audio\segment_482.wav
510
540
./data/chichewa-dataset\audio\segment_483.wav
540
570
./data/chichewa-dataset\audio\segment_484.wav
570
600
./data/chichewa-dataset\audio\segment_485.wav
600
630
./data/chichewa-dataset\audio\segment_486.wav
630
660
./data/chichewa-dataset\audio\segment_487.wav
660
690
./data/chichewa-dataset\audio\segment_488.wav
690
720
./data/chichewa-dataset\audio\segment_489.wav
720
750
./data/chichewa-dataset\audio\segment_490.wav
750
780
./data/chichewa-dataset\audio\segment_491.wav
780
810
./data/chichewa-dataset\audio\segment_492.wav
810
840
./data/chichewa-dataset\audio\segment_493.wav
840
870
./data/chichewa-dataset\audio\segment_494.wav
870
900
./data/chichewa-dataset\audio\segment_495.wav
900
930
./data/chichewa-dataset\audio\segment_496.wav
930
960
./data/chichewa-dataset\audio\segment_497.wav
960
990
./data/chichewa-dataset\audio\segment_498.wav
990
1,020
./data/chichewa-dataset\audio\segment_499.wav
1,020
1,050
./data/chichewa-dataset\audio\segment_500.wav
1,050
1,080